Onani zimene zilipo

GAWO 1

Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Paciyambi Mawu anali na Mulungu ndipo Mawuyo anali mulungu (gnj 1 00:00–00:43)

Yoh. 1:1, 2

Mawu anaseŵenzetsedwa na Mulungu polenga zinthu zonse (gnj 1 00:44–01:00)

Yoh. 1:3a

Moyo komanso kuwala zinakhalako kudzela mwa Mawu (gnj 1 01:01–02:11)

Yoh. 1:3b, 4

Mdima sunagonjetse kuwalako (gnj 1 02:12–03:59)

Yoh. 1:5

Luka akufotokoza cifukwa cimene akulembela buku lake komanso mmene zinthu zinalili pa nthawiyo. Akulembela Teofilo (gnj 1 04:13–06:02)

Luka 1:1-4

Gabirieli akukambilatu za kubadwa kwa Yohane M’batizi (gnj 1 06:04–13:53)

Luka 1:5-25

Gabirieli akukambilatu za kubadwa kwa Yesu (gnj 1 13:52–18:26)

Luka 1:26-38

Mariya wapita kukaona wacibale wake Elizabeti (gnj 1 18:27–21:15)

Luka 1:39-45

Mariya alemekeza Yehova (gnj 1 21:14–24:00)

Luka 1:46-56

Kubadwa na kupatsidwa dzina kwa Yohane (gnj 1 24:01–27:17)

Luka 1:57-66

Ulosi wa Zekariya (gnj 1 27:15–30:56)

Luka 1:67-80

Mariya wakhala na pakati mwa mphamvu ya mzimu woyela; zimene Yosefe anacitapo (gnj 1 30:58–35:29)

Yosefe na Mariya akupita ku Betelehemu; Yesu wabadwa (gnj 1 35:30–39:53)

Luka 2:1-7

Angelo aonekela kwa abusa amene ali panja (gnj 1 39:54–41:40)

Luka 2:8-14

Abusa akupita kodyetsela ziweto (gnj 1 41:41–43:53)

Luka 2:15-20

Yesu akupelekedwa kwa Yehova pa kacisi (gnj 1 43:56–45:02)

Luka 2:21-24

Simiyoni wakhala na mwayi woona Khristu (gnj 1 45:04–48:50)

Luka 2:25-35

Anna akukamba za mwanayu (gnj 1 48:52–50:21)

Luka 2:36-38

Kufika kwa okhulupilila nyenyezi komanso pulani ya Herode yakuti aphe ana (gnj 1 50:25–55:52)

Yosefe watenga Mariya na Yesu ndipo akuthaŵila nawo ku Iguputo (gnj 1 55:53–57:34)

Herode akupha ana aamuna mʼBetelehemu na mʼzigawo zake zonse (gnj 1 57:35–59:32)

Banja la Yesu lakhazikika ku Nazareti (gnj 1 59:34–1:03:55)

Mat. 2:19-23; Luka 2:39, 40

Yesu wa zaka 12 ali pa kacisi (gnj 1 1:04:00–1:09:40)

Luka 2:41-50

Yesu abwelela ku Nazareti na makolo ake (gnj 1 1:09:41–1:10:27)

Luka 2:51, 52

Kuwala kwenikweni kunali kutatsala pangʼono kubwela mʼdziko (gnj 1 1:10:28–1:10:55)

Yoh. 1:9