Tsiku Laciŵili
“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa cipulumutso cake”—Salimo 96:2
M’maŵa
-
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
-
8:30 Nyimbo Na. 53 na Pemphelo
-
8:40 ‘Niyenela Kulengeza Uthenga Wabwino wa Ufumu’ (Luka 4:43)
-
8:50 SEŴELO LALIKULU LA M’BAIBO:
Uthenga Wabwino Wolalikidwa na Yesu: Mbali 1
Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Gawo Laciŵili (Mateyu 2:1-23; Luka 2:1-38, 41-52; Yohane 1:9)
-
9:25 Nyimbo Na. 69 na Zilengezo
-
9:35 YOSIYILANA: Maulosi Okhudza Mesiya Anakwanilitsika!
-
• Pambuyo pa Mthenga (Malaki 3:1; 4:5; Mateyu 11:10-14)
-
• Anabadwa kwa Namwali (Yesaya 7:14; Mateyu 1:18, 22, 23)
-
• Anabadwila ku Betelehemu (Mika 5:2; Luka 2:4-7)
-
• Anatetezedwa Ali Mwana (Hoseya 11:1; Mateyu 2:13-15)
-
• Anachedwa Mnazareti (Yesaya 11:1, 2; Mateyu 2:23)
-
• Anafika pa Nthawi Yoikika (Danieli 9:25; Luka 3:1, 2, 21, 22)
-
-
10:40 UBATIZO: Pitilizani ‘Kugonjela Uthenga Wabwino’ (2 Akorinto 9:13; 1 Timoteyo 4:12-16; Aheberi 13:17)
-
11:10 Nyimbo Na. 24 na Kupumula
Masana
-
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
-
12:45 Nyimbo Na. 83
-
12:50 YOSIYILANA: Seŵenzetsani Uthenga Wabwino Pogonjetsa Uthenga Woipa
-
• Mijedo Yovulaza (Yesaya 52:7)
-
• Cikumbumtima Covutitsidwa (1 Yohane 1:7, 9)
-
• Zinthu Zimene Zikucitika Masiku Ano (Matthew 24:14)
-
• Zolefula (Mateyu 11:28-30)
-
-
13:35 YOSIYILANA: “Ofunitsitsa Kulengeza Uthenga Wabwino”
-
• Sinali Nchito ya Atumwi Okha (Aroma 1:15; 1 Atesalonika 1:8)
-
• Ni Mbali ya Kulambila (Aroma 1:9)
-
• Khalani Okonzeka Pokhala na Zida Zoyenela (Aefeso 6:15)
-
-
14:15 VIDIYO: Mmene ‘Uthenga Wabwino Ukubalila Zipatso na Kufalikila Padziko Lonse’ (Akolose 1:6)
-
14:40 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo
-
14:50 YOSIYILANA: Pitilizani Kulalikila Uthenga Wabwino
-
• Kulikonse Kumene Mungakhale (2 Timoteyo 4:5)
-
• Kulikonse Kumene Mulungu Angakutsogoleleni (Machitidwe 16:6-10)
-
-
15:15 Kodi Mudzacita Ciyani “Cifukwa ca Uthenga Wabwino”? (1 Akorinto 9:23; Yesaya 6:8)
-
15:50 Nyimbo Na. 21 na Pemphelo Lothela