Limbikani, Musafooke!

Onani nkhani zilipo pa tsiku lililonse, zimene zidzakuthandizani kucita coyenela na kupilila mayeselo.

Tsiku Loyamba

N’ciani cingathandize Akhristu kukulitsa makhalidwe owathandiza kupilila zovuta?

Tsiku laciŵili

Kodi Mulungu Wamphamvuyonse Amatipatsa Bwanji Mphamvu Zopilila na Kutitonthoza?

Tsiku Lacitatu

Yesu anati: “Amene adzapilile mpaka pa mapeto, ndiye amene adzapulumuke.” Mungacite ciani kuti mulabadile mau ake?

Mau kwa Osonkhana

Mwina mungakonde kupezekapo pa mamiting’i apadela amene adzacitika pamsonkhano. Mungawonenso pa pulogilamu ino ngati mufuna kudziŵa zambili zokhudza akalinde, ubatizo, zopeleka, ofesi ya cithandizo ca odwala, zotaika, malo okhala, kapena nchito yodzipeleka.