Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Loyamba

Tsiku Loyamba

“Tisaleke kucita zabwino” —AGALATIYA 6:9

KUM’MAŴA

  • 8:20 Nyimbo za Pavidiyo

  • 8:30 Nyimbo 143 na Pemphelo

  • 8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Sitifunika Kufooka—Maka-maka Lomba! (Chivumbulutso 12:12)

  • 9:15 YOSIILANA: Pitilizani Kulalikila “Mwakhama”

    • Ulaliki Wamwayi (Machitidwe 5:42; Mlaliki 11:6)

    • Kunyumba ndi Nyumba (Machitidwe 20:20)

    • Ulaliki Wapoyela (Machitidwe 17:17)

    • Kupanga Ophunzila (Aroma 1:14-16; 1 Akorinto 3:6)

  • 10:05 Nyimbo 153 na Zilengezo

  • 10:15 SEŴELO LA MAU CABE: Yehova Amapulumutsa Anthu Ake (Ekisodo 3:1-22; 4:1-9; 5:1-9; 6:1-8; 7:1-6; 14:5-10, 13-31; 15:1-21)

  • 10:45 Yehova—Citsanzo Cabwino Kwambili ca Kupilila (Aroma 9:22, 23; 15:13; Yakobo 1:2-4)

  • 11:15 Nyimbo 35 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:25 Nyimbo za Pavidiyo

  • 12:35 Nyimbo 135

  • 12:40 YOSIILANA: Pililanibe Pamene . . .

    • Akukucitilani Zopanda Cilungamo (Mateyu 5:38, 39)

    • Mukukalamba (Yesaya 46:4; Yuda 20, 21)

    • Muli na Zofooka (Aroma 7:21-25)

    • Mwapezeka m’Zocitika Zocititsa Manyazi (Agalatiya 2:11-14; Aheberi 12:5, 6, 10, 11)

    • Mwadwala kwa Nthawi Yaitali (Salimo 41:3)

    • Munataikilidwa Munthu Amene Mumakonda (Salimo 34:18)

    • Muzunzidwa (Chivumbulutso 1:9)

  • 13:55 Nyimbo 85 na Zilengezo

  • 14:05 SEŴELO: “Kumbukilani Mkazi wa Loti”—Mbali 1 (Luka 17:28-33)

  • 14:35 YOSIILANA: Kulitsani Makhalidwe Othandiza Kupilila

    • Cikhulupililo (Aheberi 11:1)

    • Khalidwe labwino (Afilipi 4:8, 9)

    • Cidziŵitso (Miyambo 2:10, 11)

    • Kudziletsa (Agalatiya 5:22, 23)

  • 15:15 Zimene Mungacite kuti ‘Musalephele Ngakhale Pang’ono’ (2 Petulo 1:5-10; Yesaya 40:31; 2 Akorinto 4:7-9, 16)

  • 15:50 Nyimbo 152 na Pemphelo Lothela