Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Khalani Wolimba!

Khalani Wolimba!

YOSWA 1:9

KUM’MAŴA

  • 8:40 Nyimbo Zamalimba

  • 8:50 Nyimbo Na. 38 na Pemphelo

  • 9:00 Yehova Ndiye Amatipatsa “Mphamvu ndi Nyonga”

  • 9:15 Khalani Wolimba—Mangani Cikhulupililo Canu

  • 9:30 Khalani Wolimba—Kangalikani pa Kulalikila, na Kuphunzitsa Ena

  • 9:55 Nyimbo Na. 7 na Zilengezo

  • 10:05 Kucoka pa Kufooka, Kukhala Wolimba!

  • 10:35 Kudzipatulila na Ubatizo

  • 11:05 Nyimbo Na. 79

KUMASANA

  • 12:20 Nyimbo Zamalimba

  • 12:30 Nyimbo Na. 102

  • 12:35 Zocitika

  • 12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:15 Yosiilana: Khalani Wolimba—Cilikizani Ucifumu wa Yehova . . .

    • Monga Wacicepele

    • Monga Okwatilana

  • 13:45 Nyimbo Na. 126 na Zilengezo

  • 13:55 “Limbani M’cikhulupililo, . . . Khalani Amphamvu”

  • 14:55 Nyimbo Na. 2 na Pemphelo