Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  1. Kodi mphamvu na nyonga tingazipeze kuti? (Yos. 1:9; Sal. 68:35)

  2. Cofunika n’ciani kuti tipitilize kumanga cikhulupililo cathu? (Aheb. 11:6)

  3. N’cifukwa ciani tili na cidalilo kuti nchito imene Yehova anatipatsa tidzaikwanitsa? (Hag. 2:4-9)

  4. Kodi Yehova amatilimbitsa bwanji pokumana na mayeselo aakulu? (Sal. 18:6, 30; Akol. 4:10, 11)

  5. N’ciani cingathandize acicepele, komanso okwatilana, kucilikiza ucifumu wa Yehova? (Mat. 22:37, 39)

  6. Kodi tingakhale bwanji ‘olimba m’cikhulupililo’ komanso “amphamvu”? (1 Akor. 16:13; Aroma 15:5; Aheb. 5:11–6:1; 12:16, 17)