Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Khalani Wolimba Mtima!

Khalani Wolimba Mtima!

SALIMO 138:3

KUM’MAŴA

  • 8:30 Nyimbo Zamalimba

  • 8:40 Nyimbo Na. 73 na Pemphelo

  • 8:50 Yehova Ndiye Amatilimbitsa Mtima

  • 9:05 Yosiilana: Khalani Wolimba Mtima Monga . . .

    • Inoki

    • Mose

    • Yehosafati

    • Petulo

  • 10:05 Nyimbo Na. 69 na Zilengezo

  • 10:15 Khalani Wolimba Mtima mu Ulaliki

  • 10:30 Kudzipatulila na Ubatizo

  • 11:00 Nyimbo Na. 48

KUMASANA

  • 12:10 Nyimbo Zamalimba

  • 12:20 Nyimbo Na. 63 na Pemphelo

  • 12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Imani ku Mbali ya Kulambila Koona

  • 13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:30 Nyimbo Na. 76 na Zilengezo

  • 13:40 Yosiilana: Tengelani Kulimba Mtima kwa Khristu Zinthu Zikavuta . . .

    • M’banja

    • Ku Sukulu

    • Ku Nchito

    • Kumene Tikhala

  • 14:40 Kulimba Mtima Kwanu ‘Kudzabweletsa Mphoto Yaikulu’

  • 15:15 Nyimbo Na. 119 na Pemphelo