Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aaya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aaya
  1. N’cifukwa ciani tiyenela kukhala na cidalilo popempha Yehova kuti atipatse kulimba mtima? (Sal. 138:3)

  2. Kodi tingatengele bwanji kulimba mtima kwa atumiki a Mulungu a m’nthawi zakale? (Mac. 4:31)

  3. Nanga tingakhale bwanji olimba mtima mu ulaliki? (1 Ates. 2:2)

  4. Cimatithandiza n’ciani kukhalabe olimba mtima zinthu zikakhala zovuta? (1 Pet. 2:21-23)

  5. Kodi kulimba mtima kwathu kwacikhristu kuli na madalitso anji? (Aheb. 10:35)