Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  1. Kodi tingaonetse bwanji cikondi cathu pa Mulungu? (Deut. 13:3, 4; 1 Yoh. 5:3)

  2. N’cifukwa ciani tifunika kukonda abale athu? (1 Yoh. 4:11, 20, 21)

  3. Kodi tingaonetse bwanji cikondi pa anthu anzathu? (Lev. 19:18; Aef. 5:29)

  4. Kodi tingaonetse bwanji kuti timatengela cikondi ca Yehova? (1 Pet. 4:8; Akol. 3:13)

  5. N’ciani cingatithandize kutamanda Yehova? (Sal. 104:33; 146:2, 5)

  6. Kodi kukonda Yehova na mtima wathu wonse kumatanthauza ciani? (Eks. 34:14; Amosi 5:15; Aroma 12:11)