Pulogilamu ya Msonkhano Wadela wa mu 2020-2021—Wa Woyang’anila Dela

Seŵenzetsani kapulogilamu kano pa msonkhano wadela. Mutu wa msonkhano wadela ni wakuti: ‘Kondweletsani Mtima wa Yehova.’

Kondweletsani Mtima wa Yehova

Pulogilamu ya kum’maŵa na kumasana ya msonkhano wadela wa woyang’anila dela.

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Mafunso amenewa adzayankhidwa pa msonkhano wadela umenewu.