Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  1. 1. Ni mwayi wotani umene tili nawo monga atumiki a Yehova? (Miy. 27:11)

  2. 2. Kodi tingatengele bwanji citsanzo ca Yesu kuti tikondweletse mtima wa Yehova? (Yoh. 8:29)

  3. 3. Tingakondweletse bwanji mtima wa Yehova pamene tilalikila? (Yoh. 15:8)

  4. 4. Kodi tingam’kondweletse bwanji Yehova m’mbali zonse za umoyo wathu? (Yoh. 14:31; Aef. 6:1-4; Sal. 35:18; 1 Pet. 2:12)

  5. 5. N’ciani cingatithandize kupilila zovuta, zolefula, na mayeselo? (Neh. 8:10)