Njila ya Kumoyo Wamuyaya—Kodi Mwaipeza?

Padzikoli pali zipembedzo ziŵili cabe. Cimene cimatsogolela kumoyo komanso cotsogolela kuciwonongeko. Bulosha iyi ingakuthandizeni kupeza njila yotsogolela kumoyo wamuyaya.

Mau Oyamba

Miyoyo yathu, tsopano ndi m’tsogolo, umadalila Mulungu Wamphamvuzonse. Conco n’cinthu cofunika kwambili kuti kulambila kwathu kukhale kovomelezeka kwa iye!

MBALI 1

Kodi Zipembedzo Zonse Zimaphunzitsa Zoona?

Azipembedzo amakhulupilila zambili zosiyana-siyana. Koma kodi zonsezo zimagwilizana ndi coonadi?

MBALI 2

Kodi Tingadziŵe Bwanji Zoona za Mulungu?

Kodi ulipo muyezo umene anthu angagwilizanepo za cipembedzo coona?

MBALI 3

Ndani Amene Ali ku Malo a Mizimu?

Zikhulupililo zamizimu n’zomphamvu kwambili m’zipembedzo. Koma kodi zimaphunzitsa zoona? Baibulo limapeleka yankho

MBALI 4

Kodi Makolo Athu Anapita Kuti?

Ambili amakhulupilila kuti imfa si mapeto a moyo, koma ciyambi ca moyo wina. Kodi Baibo imakamba kuti bwanji?

MBALI 5

Kudziŵa Zoona pa Nkhani ya Matsenga ndi Ufiti

Mizimu yoipa ndi yamphamvu komanso yoopsa, komabe tisamaiope mopambanitsa

MBALI 6

Kodi Mulungu Amavomeleza Zipembedzo Zonse?

Anthu ena amaganiza kuti zipembedzo zonse zimakondweletsa Mulungu. Kodi n’zimene Baibulo limaphunzitsa?

MBALI 7

Kodi Amene Ali m’Cipembedzo Coona Ndani?

Baibulo lingakuthandizeni kudziŵa amene amacita cifunilo ca Mulungu?

MBALI 8

cokani-m’cipembedzo-conama-loŵani-m’cipembedzo-coona

Yesu anati: “Amene sali kumbali yanga ndi wotsutsana ndi ine.” Kodi mungaonetse bwanji mbali imene mwaimako?

PART 9

True Religion Can Benefit You Forever!

If you worship Jehovah, he will bless you now and in the future.