Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Laciŵili

Tsiku Laciŵili

‘Kuonetsa kulimba mtima kowonjezeleka polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha’ —AFILIPI 1:14

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 76 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIILANA: Khalani Olimba Mtima . . .

    • Inu Ophunzila Baibo (Machitidwe 8:35, 36; 13:48)

    • Inu Acicepele (Salimo 71:5; Miyambo 2:11)

    • Inu Ofalitsa (1 Atesalonika 2:2)

    • Inu Okwatilana (Aefeso 4:26, 27)

    • Inu Makolo (1 Samueli 17:55)

    • Inu Apainiya (1 Mafumu 17:6-8, 12, 16)

    • Akulu mu Mpingo (Machitidwe 20:28-30)

    • Inu Okalamba (Danieli 6:10, 11; 12:13)

  • 9:50 Nyimbo Na. 119 na Zilengezo

  • 10:00 YOSIILANA: Titengele Citsanzo ca Anthu Olimba Mtima, Osati Amantha!

    • Osati ca Akalonga 10 aja, Koma ca Yoswa na Kalebe (Numeri 14:7-9)

    • Osati ca Anthu a ku Merozi, Koma ca Yaeli (Oweruza 5:23)

    • Osati Aneneli Onama, Koma Mikaya (1 Mafumu 22:14)

    • Osati ca Uliya, Koma ca Yeremiya (Yeremiya 26:21-23)

    • Osati ca Wolamulila Wacuma Wacinyamata, Koma ca Paulo (Maliko 10:21, 22)

  • 10:45 UBATIZO: “Ife si Mtundu wa Anthu Obwelela M’mbuyo”! (Aheberi 10:35, 36, 39; 11:30, 32-34, 36; 1 Petulo 5:10)

  • 11:15 Nyimbo Na. 38 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 111

  • 12:50 YOSIILANA: Tiphunzile Kulimba Mtima ku Zolengedwa

    • Mkango (Mika 5:8)

    • Mahosi (Yobu 39:19-25)

    • Mshulu [kanyama] (Salimo 91:3, 13-15)

    • Cozo [kambalame] (1 Petulo 3:15)

    • Njovu (Miyambo 17:17)

  • 13:40 Nyimbo Na. 60 na Zilengezo

  • 13:50 YOSIILANA: Mmene Abale Athu Amaonetsela Kulimba Mtima . . .

    • Mu Africa (Mateyu 10:36-39)

    • Ku Asia (Zekariya 2:8)

    • Ku Europe (Chivumbulutso 2:10)

    • Ku North America (Yesaya 6:8)

    • Ku Oceania (Salimo 94:14, 19)

    • Ku South America (Salimo 34:19)

  • 15:15 Khalani Olimba Mtima Koma Osati Odzidalila (Miyambo 3:5, 6; Yesaya 25:9; Yeremiya 17:5-10; Yohane 5:19)

  • 15:50 Nyimbo Na. 3 na Pemphelo Lothela