Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Lacitatu

Tsiku Lacitatu

“Limba mtima ndipo ucite zinthu mwamphamvu. Yembekezela Yehova” —SALIMO 27:14

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 73 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIILANA: Zocitika Zam’tsogolo Zimene Zidzafuna Kulimba Mtima

    • Kulengeza “Bata ndi Mtendele!” (1 Atesalonika 5:2, 3)

    • Kuwonongedwa kwa Babulo Wamkulu (Chivumbulutso 17:16, 17)

    • Kulengeza Uthenga wa Matalala (Chivumbulutso 16:21)

    • Kuukila kwa Gogi wa Magogi (Ezekieli 38:10-12, 14-16)

    • Aramagedo (Chivumbulutso 16:14, 16)

    • Nchito Yaikulu Yokonzanso Zinthu (Yesaya 65:21)

    • Ciyeso Cotsiliza (Chivumbulutso 20:3, 7, 8)

  • 10:10 Nyimbo Na. 8 na Zilengezo

  • 10:20 NKHANI YA ANTHU ONSE: Kodi Ciyembekezo ca Ciukililo Cimatithandiza Bwanji Kukhala Olimba Mtima? (Maliko 5:35-42; Luka 12:4, 5; Yohane 5:28, 29; 11:11-14)

  • 10:50 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 11:20 Nyimbo Na. 151 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 5

  • 12:50 FILIMU YAIKULU: Nkhani ya Yona—Kutengapo Phunzilo pa Kulimba Mtima na Cifundo (Yona 1-4)

  • 13:40 Nyimbo Na. 71 na Zilengezo

  • 13:50 Ali ku Mbali Yathu ni Ambili Kuposa Adani Athu! (Deuteronomo 7:17, 21; 28:2; 2 Mafumu 6:16; 2 Mbiri 14:9-11; 32:7, 8, 21; Yesaya 41:10-13)

  • 14:50 Nyimbo na Pemphelo Lothela