Tsiku Loyamba
‘Khalani wolimba mtima kwambili’ —YOSWA 1:7
KUM’MAŴA
-
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
-
8:30 Nyimbo Na. 110 na Pemphelo
-
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Yehova Ndiye Gwelo la Kulimba Mtima Kwazoona (Salimo 28:7; 31:24; 112:7, 8; 2 Timoteyo 1:7)
-
9:10 YOSIILANA: Cimene Akhristu Oona Afunikila Kukhala Olimba Mtima
-
Polalikila (Chivumbulutso 14:6)
-
Kuti Akhalebe Oyela (1 Akorinto 16:13, 14)
-
Kuti Asamatengeko Mbali M’zandale (Chivumbulutso 13:16, 17)
-
-
10:05 Nyimbo Na. 126 na Zilengezo
-
10:15 KUŴELENGA BAIBO MWAUMOYO: “Limba Mtima, Ugwile Nchitoyi Mwamphamvu”! (1 Mbiri 28:1-20; 1 Samueli 16:1-23; 17:1-51)
-
10:45 “Cida Ciliconse Cimene Cidzapangidwe Kuti Cikuvulaze Sicidzapambana” (Yesaya 54:17; Salimo 118:5-7)
-
11:15 Nyimbo Na. 61 na Kupumula
KUMASANA
-
12:25 Vidiyo ya Nyimbo
-
12:35 Nyimbo Na. 69
-
12:40 YOSIILANA: Zofooketsa, Motsutsana ndi Zothandiza Kukhala Olimba Mtima
-
Kutaya Mtima, Motsutsana ndi Ciyembekezo (Salimo 27:13, 14)
-
Kudandaula, Motsutsana ndi Kuyamikila (Salimo 27:1-3)
-
Zosangalatsa Zosayenela, Motsutsana ndi Utumiki Wakumunda (Salimo 27:4)
-
Mayanjano Oipa, Motsutsana ndi Mayanjano Abwino (Salimo 27:5; Miyambo 13:20)
-
Nzelu za Dziko, Motsutsana ndi Phunzilo Laumwini (Salimo 27:11)
-
Zikaikilo, Motsutsana ndi Cikhulupililo (Salimo 27:7-10)
-
-
14:10 Nyimbo Na. 55 na Zilengezo
-
14:20 YOSIILANA: Zimene Anaika Paciswe; Mmene Anawadalitsila
-
Hananiya, Misayeli, ndi Azariya (Danieli 1:11-13; 3:27-29)
-
Akula na Purisikila (Aroma 16:3, 4)
-
Sitefano (Machitidwe 6:11, 12)
-
-
14:55 “Limbani mtima! Ndaligonjetsa Dziko Ine” (Yohane 16:33; 1 Petulo 2:21, 22)
-
15:15 Asilikali Olimba Mtima a Khristu (2 Akorinto 10:4, 5; Aefeso 6:12-18; 2 Timoteyo 2:3, 4)
-
15:50 Nyimbo Na. 22 na Pemphelo Lothela