Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela wa 2017-2018—Wa Woimila Nthambi

Onani ndandanda ya msonkhano wa delawu, wa nkhani ya woimila nthambi.

Musaleme pa Kukwanilitsa Cilamulo ca Khristu!

Msonkhanowu udzatithandiza kudziŵa kuti Cilamulo ca Khristu n’ciani, na mmene tingacikwanilitsile.

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Mafunso aya adzayankhiwa pa msonkhano wa delawu.