Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Musaleme pa Kucita Zabwino!

Musaleme pa Kucita Zabwino!

KUM’MAŴA

  • 8:30 Nyimbo

  • Zamalimba 8:40 Nyimbo Na. 77 na Pemphelo

  • 8:50 N’cifukwa Ninji Kucita Zabwino Kumakhala Kovuta?

  • 9:05 Yosiilana: Pewani Kufesela ku Thupi

    • Muziseŵenzetsa Mwanzelu ma Webusaiti a Maceza

    • Muzisankha Zosangalatsa Zabwino

    • Pewani Mzimu wa Kaduka

    • Konzani Tsogolo Lodalilika

  • 10:05 Nyimbo Na. 45 na Zilengezo

  • 10:15 Pitilizani Kucitila Onse Zabwino

  • 10:30 Kudzipeleka na Ubatizo

  • 11:00 Nyimbo Na. 63

KUMASANA

  • 12:10 Nyimbo Zamalimba

  • 12:20 Nyimbo Na. 127 na Pemphelo

  • 12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Pewani Kuyesa Kupusitsa Mulungu—Motani?

  • 13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:30 Nyimbo Na. 59 na Zilengezo

  • 13:40 Yosiilana: Pitilizani Kufesela ku Mzimu

    • Kulitsani Cizoloŵezi Coŵelenga

    • Muzilola Mfundo za M’Baibo Kukutsogolelani

    • ‘Dzanja Lanu Lisapumule’

  • 14:40 Zimene Tidzatuta Tikapanda Kulema

  • 15:15 Nyimbo Na. 126 na Pemphelo