Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Laciŵili

Tsiku Laciŵili

“YENDANIBE M’CIKONDI”​—AEFESO 5:2

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 85 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIILANA: Onetsani Cikondi Cosatha mu Mpingo

    • Kwa Amene Akutsogolela (1 Atesalonika 5:12, 13)

    • Kwa Akazi Amasiye ndi Ana Amasiye (Yakobo 1:27)

    • Kwa Okalamba (Levitiko 19:32)

    • Kwa Atumiki Anthawi Zonse (1 Atesalonika 1:3)

    • Kwa Alendo Ocokela ku Maiko Ena (Levitiko 19:34; Aroma 15:7)

  • 9:50 Nyimbo Na. 58 na Zilengezo

  • 10:00 YOSIILANA: Onetsani Cikondi Cosatha mu Ulaliki

    • Mwa Kuonetsa Cikondi Canu pa Mulungu (1 Yohane 5:3)

    • ‘Uzikonda Mnansi Wako Mmene Udzikondela Wekha’ (Mateyu 22:39)

    • Muzikonda Mawu a Yehova (Salimo 119:97; Mateyu 13:52)

  • 10:45 UBATIZO: Phunzilani Khalidwe la Cikondi kwa Yesu (Mateyu 11:28-30)

  • 11:15 Nyimbo Na. 52 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 84

  • 12:50 YOSIILANA: Mmene Abale Athu Amaonetsela Cikondi Cosatha . . .

    • mu Africa (Genesis 16:13)

    • ku Asia (Machitidwe 2:44)

    • ku Europe (Yohane 4:35)

    • ku North America (1 Akorinto 9:22)

    • ku Oceania (Salimo 35:18)

    • ku South America (Machitidwe 1:8)

  • 13:55 YOSIILANA: Onetsani Cikondi Cosatha M’banja

    • Muzim’konda Mkazi Wanu (Aefeso 5:28, 29)

    • Muzim’konda Mwamuna Wanu (Aefeso 5:33; 1 Petulo 3:1-6)

    • Muziŵakonda Ana Anu (Tito 2:4)

  • 14:35 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo

  • 14:45 FILIMU YAIKULU: Nkhani ya Yosiya: Kondani Yehova; Danani Naco Coipa—Gawo I (2 Mbiri 33:10-24; 34:1, 2)

  • 15:15 Phunzitsani Ana Anu Kuonetsa Ena Cikondi (2 Timoteyo 3:14, 15)

  • 15:50 Nyimbo Na. 134 na Pemphelo Lothela