Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Lacitatu

Tsiku Lacitatu

“PITILIZANI KUCITA ZINTHU ZIMENE ZINGACITITSE MULUNGU KUKUKONDANI”​—YUDA 21

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 106 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIILANA: Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili

    • N’coleza Mtima Ndiponso N’cokoma Mtima (1 Akorinto 13:4)

    • Sicicita Nsanje; Sicidzitama (1 Akorinto 13:4)

    • Sicidzikuza; Sicicita Zosayenela (1 Akorinto 13:4, 5)

    • Sicisamala Zofuna Zake Zokha; Sicikwiya (1 Akorinto 13:5)

    • Sicisunga Zifukwa; Sicikondwela ndi Zosalungama (1 Akorinto 13:5, 6)

    • Cimakondwela ndi Coonadi; Cimakwilila Zinthu Zonse (1 Akorinto 13:6, 7)

    • Cimakhulupilila Zinthu Zonse; Cimayembekezela Zinthu Zonse (1 Akorinto 13:7)

    • Cimapilila Zinthu Zonse; Cikondi Sicitha (1 Akorinto 13:7, 8)

  • 10:10 Nyimbo Na. 150 na Zilengezo

  • 10:20 NKHANI YA ANTHU ONSE: Cikondi ca Zoona Cimapezeka M’dzikoli Lodzala Cidani—Koma Kuti? (Yohane 13:34, 35)

  • 10:50 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 11:20 Nyimbo Na. 1 na Kupumula

KUMASANA