Tsiku Loyamba
“MULUNGU AMAKUPHUNZITSANI KUKONDANA”—1 1 ATESALONIKA 4:9
KUM’MAŴA
-
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
-
8:30 Nyimbo Na. 105 na Pemphelo
-
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: “Cikondi Sicitha”—Motani? (Aroma 8:38, 39; 1 Akorinto 13:1-3, 8, 13)
-
9:15 YOSIILANA: Samalani Kuti Musadalile Zinthu Zosakhalitsa
-
Cuma (Mateyu 6:24)
-
Kuchuka (Mlaliki 2:16; Aroma 12:16)
-
Nzelu za Anthu (Aroma 12:1, 2)
-
Mphamvu na Kukongola (Miyambo 31:30; 1 Petulo 3:3, 4)
-
-
10:05 Nyimbo Na. 40 na Zilengezo
-
10:15 KUŴELENGA BAIBO MWAUMOYO: Yehova Anapitilizabe Kuonetsa Kukoma Mtima Kosatha (Genesis 37:1-36; 39:1–47:12)
-
10:45 Yehova Amakonda Aja Okonda Mwana Wake (Mateyu 25:40; Yohane 14:21; 16:27)
-
11:15 Nyimbo Na. 20 na Kupumula
KUMASANA
-
12:25 Vidiyo ya Nyimbo
-
12:35 Nyimbo Na. 107
-
12:40 YOSIILANA: Cikondi Sicitha Olo Kuti . . .
-
Tinakulila M’banja Lopanda Cikondi (Salimo 27:10)
-
Anzanu ku Nchito Alibe Cikondi (1 Petulo 2:18-20)
-
Anzanu ku Sukulu Ali na Makhalidwe Oipa (1 Timoteyo 4:12)
-
Mudwala Matenda Osatha (2 Akorinto 12:9, 10)
-
Ndimwe Osauka (Afilipi 4:12, 13)
-
Mutsutsidwa M’banja (Mateyu 5:44)
-
-
13:50 Nyimbo Na. 141 na Zilengezo
-
14:00 YOSIILANA: Cilengedwe Cimaonetsa Cikondi ca Yehova
-
Za Kuthambo (Salimo 8:3, 4; 33:6)
-
Dziko Lapansi (Salimo 37:29; 115:16)
-
Zomela (Genesis 1:11, 29; 2:9, 15; Machitidwe 14:16, 17)
-
Nyama (Genesis 1:27; Mateyu 6:26)
-
Thupi la Munthu (Salimo 139:14; Mlaliki 3:11)
-
-
14:55 “Yehova Amalanga Aliyense Amene Iye Amamukonda” (Aheberi 12:5-11; Salimo 19:7, 8, 11)
-
15:15 “Valani Cikondi” (Akolose 3:12-14)
-
15:50 Nyimbo Na. 130 na Pemphelo Lothela