Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Laciŵili

Tsiku Laciŵili

“Nyadilani dzina lake loyela. Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale”​—Salimo 105:3

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 53 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIILANA: Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila​—Nolani Maluso Anu

    • • Kufunsa Mafunso (Yakobo 1:19)

    • • Lolani Mphamvu ya Mawu a Mulungu Kugwila Nchito (Aheberi 4:12)

    • • Kuseŵenzetsa Mafanizo Pofotokoza Mfundo Zofunika Kwambili (Mateyu 13:34, 35)

    • • Kukamba Mwaumoyo Pophunzitsa (Aroma 12:11)

    • • Kuonetsa Cifundo (1 Atesalonika 2:7, 8)

    • • Kuŵafika pa Mtima Anthu (Miyambo 3:1)

  • 9:50 Nyimbo Na. 58 na Zilengezo

  • 10:00 YOSIILANA: Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila​—Landilani Thandizo la Yehova

    • • Zida Zofufuzila (1 Akorinto 3:9; 2 Timoteyo 3:16, 17)

    • • Abale Athu (Aroma 16:3, 4; 1 Petulo 5:9)

    • • Pemphelo (Salimo 127:1)

  • 10:45 UBATIZO: Mmene Ubatizo Wanu Ungakubweletseleni Cimwemwe Cacikulu (Miyambo 11:24; Chivumbulutso 4:11)

  • 11:15 Nyimbo Na. 79 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 76

  • 12:50 Mmene Abale Athu Akupezela Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila . . .

    • • mu Africa

    • • ku Asia

    • • ku Europe

    • • ku North America

    • • ku Oceania

    • • ku South America

  • 13:35 YOSIILANA: Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo . . .

    • • Kudzidyetsa Okha Kuuzimu (Mateyu 5:3; Yohane 13:17)

    • • Kumapezeka pa Misonkhano (Salimo 65:4)

    • • Kupewa Mayanjano Oipa (Miyambo 13:20)

    • • Kuleka Makhalidwe Odetsa (Aefeso 4:22-24)

    • • Kukhala pa Ubale Wolimba na Yehova (1 Yohane 4:8, 19)

  • 14:30 Nyimbo Na. 110 na Zilengezo

  • 14:40 SEŴELO LA M’BAIBO: Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”​—Gawo 1 (Nehemiya 1:1–6:19)

  • 15:15 Kupanga Ophunzila Pali Pano, Kumatikonzekeletsa Kukapanga Ophunzila m’Dziko Latsopano (Yesaya 11:9; Machitidwe 24:15)

  • 15:50 Nyimbo Na. 140 na Pemphelo Lothela