NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA January 2016

Maganiziyi ili ndi nkhani zophunzila mlungu wa February 29 mpaka April 3, 2016.

‘Pitilizani Kukonda Abale’

Lemba la caka ca 2016 lingatithandize kukonzekela zinthu zimene zidzacitika posacedwapa.

Muzilimbikitsidwa ndi Mphatso ya Mulungu Yosatheka Kuifotokoza

Kodi cikondi ca Mulungu cimatilimbikitsa bwanji kutsatila Yesu mosamala, kuonetsa cikondi kwa abale athu, ndiponso kukhululukila ena?

Mzimu Umacitila Umboni Limodzi ndi Mzimu Wathu

Kodi kukhala wodzozedwa kumatanthauza ciani? Kodi munthu amadzozedwa bwanji?

“Tipita Nanu Limodzi”

N’ciani cimene tiyenela kukumbukila pa nkhani ya a 144,000?

Kugwila Nchito ndi Mulungu Kumabweletsa Cimwemwe

Kodi kugwila nchito ndi Yehova kumatibweletsela bwanji cimwemwe ndi citetezo cakuuzimu?