Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Xuanyu Han/Moment via Getty Images

M’kope ino ya Galamuka!

M’kope ino ya Galamuka!

Dziko lapansi lili pa ciwopsezo.

Kodi lidzapulumuka, kapena tidzawonongekela nalo limodzi? Ŵelengani nkhani zili pansipa kuti mudziŵe zimene zikucitikila dziko lapansi na kuona ngati pali zifukwa zokhalila na ciyembekezo.

Kodi m’tsogolo n’ciyani cidzacitikila

  • Madzi Abwino?

  • Nyanja Zamcele?

  • Nkhalango?

  • Mpweya?