Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mawu Oyamba

Mawu Oyamba

Zinthu 6 Zimene Ana Afunika Kuphunzila

Kodi mwana wanu akadzakula, mungakonde kuti akakhale munthu wotani?

  • Wodziletsa

  • Wodzicepetsa

  • Wolimbikila

  • Waudindo

  • Wokhwima m’Maganizo

  • Woona mtima

Ana sangakhale na makhalidwe amenewa paokha. Afunikila thandizo lanu.

Magazini ino idzafotokoza zinthu 6 zimene mufunika kuphunzitsa ana anu kuti akule bwino.