NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA April 2017
Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya May 29 mpaka July 2, 2017.
“Muzikwanilitsa Zimene Mwalonjeza”
Kodi lonjezo n’ciani? Kodi Malemba amakamba ciani pankhani yopanga malonjezo kwa Mulungu?
Kodi Cidzacokapo N’ciani Ufumu wa Mulungu Ukadzabwela?
Baibo imakamba kuti “Dziko likupita.” Koma, kodi “dziko” limeneli liphatikizapo ciani?
MBILI YANGA
N’natsimikiza Mtima Kukhala Msilikali wa Khristu
Demetrius Psarras anaikidwa m’ndende cifukwa cokana kumenya nkhondo. Ngakhale kuti anakumana ndi mavuto aakulu, anapitilizabe kutamanda Mulungu.
“Woweluza wa Dziko Lonse” Amacita Cilungamo Nthawi Zonse
N’cifukwa ciani tingakambe kuti Mulungu sangacite zinthu zopanda cilungamo? N’cifukwa ciani kudziŵa mfundo imeneyi n’kofunika kwa Akhristu masiku ano?
Kodi Mumacita Zinthu Mogwilizana ndi Cilungamo ca Yehova?
Kudzicepetsa na kukhala na mtima wokhululuka n’zofunika kuti ticite zinthu mogwilizana ndi cilungamo ca Yehova. Cifukwa ciani?
Yehova Atamandike Cifukwa ca Kudzipeleka Kwanu!
Mulungu Wamphamvuyonse amayamikila zimene atumiki ake amacita pokwanilitsa colinga cake, olo zitakhala zocepa.