NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2017

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya January 29-February 25, 2018.

“Ndidziŵa Kuti Adzauka”

Tingatsimikize bwanji kuti m’tsogolo kudzakhala kuuka kwa akufa?

“Ine Ndili Ndi Ciyembekezo mwa Mulungu”

N’cifukwa ciani ciphunzitso ca kuuka kwa akufa n’cofunika ngako pa cikhulupililo ca Mkhristu?

Kodi Mukumbukila?

Kodi munaŵelenga na kumvetsa bwino-bwino magazini aposacedwa a Nsanja ya Mlonda? Ngati n’conco, ni mafunso angati ozikidwa pa Baibo amene mungakwanitse kuyankha?

Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga

M’nthawi ya Aisiraeli, kodi kukhala pa mzela wa makolo a Mesiya kunadalila kukhala oyamba kubadwa?

Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga

Kodi Akhristu okwatilana ayenela kuona kuti kuseŵenzetsa kacipangizo koika m’cibalilo kochedwa IUD ni njila ya cilezi yogwilizana na Malemba?

Makolo—Thandizani Ana Anu Kupeza ‘Nzelu Zowathandiza Kuti Akapulumuke’

Makolo ambili acikhristu amakhala na nkhawa ngati mwana wawo wasankha kuti adzipeleke na kubatizika. Kodi makolo angawathandize bwanji ana awo kukula mwauzimu kuti akapulumuke?

Acicepele—“Pitilizani Kukonza Cipulumutso Canu”

Ubatizo ni cosankha cacikulu, koma acicepele sayenela kuopa kubatizidwa.

MBILI YANGA

N’nasiya Zinthu Zina Pofuna Kutsatila Ambuye

Felix Fajardo anali cabe na zaka 16 pamene anasankha kukhala Mkhristu. Tsopano papita zaka zoposa 70, ndipo saona kuti analakwitsa kutsatila Khristu kulikonse kumene anamulamula kupita.

Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2017

Mlongoza nkhani uyu adzakuthandizani kudziŵa pamene mungapeze nkhani zosiyana-siyana zimene zinafalitsidwa m’magazini a Nsanja ya Mlonda a mu 2017.