Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2017

Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2017

Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo

BAIBO

  • Umboni Winanso (Tatenai analikodi), Na. 3

  • Elias Hutter na ma Baibo Ake a Ciheberi, Na. 4

  • Pindulani na Zimene Mumaŵelenga m’Baibo, Na. 1

  • Kuphonya pa Kamvedwe, Na. 1

  • N’cifukwa Ciani Pali Osiyana-siyana? Na. 6

BAIBO IMASINTHA ANTHU

  • N’nali Kukhulupilila Kuti Kulibe Mulungu (A. Golec), Na. 5

  • N’nali Kuopa Imfa (Y. Quarrie), Na. 1

  • N’nali Kukonda Baseball Kuposa Cina Ciliconse (S. Hamilton), Na. 3

UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU

  • Kupatsa Kumapindulitsa, Na. 2

  • Kuti Munthu Akhale Mtumiki, Kodi Afunika Kukhala Wosakwatila? Na. 2

  • Kodi Akhristu Ayenela Kukondwelela Khrisimasi? Na. 6

  • Cikondi—Khalidwe Lamtengo Wapatali, Aug.

  • Kuona Zolakwa Moyenelela, Na. 6

  • Kuthetsa Mkangano ndi Kulimbikitsa Mtendele, June

  • Pakacitika Zinthu Zimene Zingasokoneze Ubwenzi, Mar.

  • Kupambana Nkhondo Yoteteza Maganizo Anu, July

YEHOVA

  • Kodi Mudzalandila Mphatso ya Mulungu Yopambana Zonse? Na. 2

  • Ndiye Amacititsa Mavuto? Na. 1

MBONI ZA YEHOVA

  • Kujaila mu Mpingo Wanu Watsopano, Nov.

  • “Wopatsa Mowolowa Manja Adzadalitsidwa” (zopeleka), Nov.

  • Umoyo Wosalila Zambili Umabweletsa Cimwemwe, May

  • “Khote-khote Ngwanjila, Palinga Mtima Mpomwepo” (Australia), Feb.

  • Anadzipeleka ku Turkey, July

  • Anadzipeleka na Mtima Wonse (alongo osakwatiwa), Jan.

  • Kuonetsa Kukoma Mtima Kamodzi Cabe, Oct.

  • “N’liti Pamene Tidzakhala na Msonkhano Wina Waukulu?” (Mexico), Aug.

  • ‘Cangu na Cikondi Zinawonjezeka Kwambili’ (msonkhano wacigawo mu 1922), May

YESU KHRISTU

  • Kodi Yesu Ananyoza Pokamba Fanizo la “Tiagalu”? Na. 5

  • Kodi Yesu Anali Kuoneka Bwanji Kweni-kweni? Na. 6

MBILI YANGA

  • Kukhala Wogontha Sikunanilepheletse Kuphunzitsa Ena (W. Markin), May

  • Kucita Zimene Yehova Watilamula Kumabweletsa Madalitso (O. Matthews), Oct.

  • N’natsimikiza Mtima Kukhala Msilikali wa Khristu (D. Psarras), Apr.

  • Kupilila Ziyeso Kumabweletsa Madalitso (P. Sivulsky), Aug.

  • Nakhala na Mwayi Wotumikila Pamodzi ndi Amuna Auzimu (D. Sinclair), Sept.

  • Napindula Cifukwa Coyenda ndi Anthu Anzelu (W. Samuelson), Mar.

  • N’nasiya Zinthu Zina Pofuna Kutsatila Ambuye (F. Fajardo), Dec.

  • Tinaona Cisomo ca Mulungu m’Njila Zambili (D. Guest), Feb.

NKHANI ZOSIYANA-SIYANA

  • Kodi Angelo Aliko Zoona? Na. 5

  • Nkhawa, Na. 4

  • Mphatso Yoposa Zonse, Na. 6

  • Dzina la m’Baibo pa Mtsuko Wakale, Mar.

  • “Udalitsike Cifukwa ca Kulingalila Bwino Kwako” (Abigayeli), June

  • Kumasuka mu Ukapolo, Na. 2

  • Zidzatheka Kuti Padzikoli Pakhale Mtendele? Na. 5

  • Kodi zidzatheka kuti padziko lapansi pakhale cilungamo ceni-ceni? Na. 3

  • Amuna Anayi Okwela pa Mahosi, Na. 3

  • Mulungu Anamucha Mfumukazi (Sara), Na. 5

  • Kacilembo Kocepetsetsa Kaciheberi, Na. 4

  • ‘Mulungu Anakondwela Naye’ (Inoki), Na. 1

  • Mmene Gayo Anathandizila Abale Ake, May

  • Kodi Moto Unali “Kunyamuliwa” Bwanji M’nthawi Zakale? Jan.

  • Yosefe wa ku Arimateya, Oct.

  • Kodi Tili mu “Masiku Otsiliza”? Na. 2

  • Musamaone Cabe Maonekedwe, June

  • Paradaiso Padziko Lapansi—Ni Yeni-yeni Kapena ni Maloto Cabe? Na. 4

  • Malangizo a Paulo Akuti Asapitilize Ulendo wa Pamadzi (Mac. 27), Na. 5

  • Mavuto, Na. 1

  • Kodi Amalonda Amene Anali Kugulitsa Ziweto M’kacisi Anali “Acifwamba”? June

  • “Ndiwe Mkazi Wokongola m’Maonekedwe Ako” (Sara), Na. 3

  • Kodi Aramagedo n’ciani? Na. 6

  • Kodi Ayuda Anali na Cizoloŵezi Canji Cimene Cinapangitsa Yesu Kuwaletsa Kulumbila? Oct.

  • Kodi Baibo Imati Ciani pa Nkhani ya Moyo na Imfa? Na. 4

  • Munthu Amene Mukonda Akadwala Matenda Osacilitsika, Na. 4

MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA

  • Yehova “sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapilile” (1 Akor. 10:13), Feb.

  • Kodi n’koyenela Mkhristu kukhala na mfuti yodzitetezela kwa anthu ena? July

  • Kodi Kukhala pa Mzela wa Makolo a Mesiya Kunadalila Kukhala Oyamba Kubadwa? Dec.

  • Kodi Akhristu apabanja ayenela kuona kuti kuseŵenzetsa ma IUD ni njila ya cilezi yogwilizana na Malemba? Dec.

  • N’cifukwa ciani zimene Mateyu na Luka analemba zokhudza umoyo wa Yesu ali mwana zimasiyana? Aug.

NKHANI ZOPHUNZILA

  • Kodi Mumathaŵila kwa Yehova? Nov.

  • Kodi Mudzayembekezela Moleza Mtima? Aug.

  • ‘Limba Mtima, Ugwile Nchito Mwamphamvu,’ Sept.

  • Magaleta na Cisoti Cacifumu Zimakutetezani, Oct.

  • Phunzilani Kukhala Wodziletsa, Sept.

  • Musalole Kuti Cikondi Canu Cizilale, May

  • “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?” May

  • Kodi Mumacita Zinthu Mogwilizana ndi Cilungamo ca Yehova? Apr.

  • Khalani ndi Cikhulupililo Ndipo Muzipanga Zosankha Mwanzelu, Mar.

  • Muzilemekeza Amene Afunika Kulandila Ulemu, Mar.

  • Kuthandiza Alendo Ocokela ku Mayiko Ena “Kutumikila Yehova Mokondwela,” May

  • Kuthandiza Ana a Alendo Ocokela m’Dziko Lina, May

  • Mmene Timavalila Umunthu Watsopano ndi Kusauvulanso, Aug.

  • Mmene Timavulila Umunthu Wakale ndi Kusauvalanso, Aug.

  • “Ine Ndili Ndi Ciyembekezo mwa Mulungu,” Dec.

  • “Ndidziŵa Kuti Adzauka,” Dec.

  • Tengelani Khalidwe la Yehova la Cifundo, Sept.

  • Tengelani Cilungamo ca Yehova na Cifundo Cake, Nov.

  • Yehova Amatsogolela Anthu Ake, Feb.

  • Yehova Amatitonthoza m’Masautso Athu Onse, June

  • Colinga ca Yehova Cidzakwanilitsika, Feb.

  • Muziika Maganizo Anu pa Nkhani Yaikulu, June

  • Musalole Ciliconse Kukumanitsani Mphoto, Nov.

  • “Tizisonyezana Cikondi Ceni-ceni m’Zocita Zathu,” Oct.

  • Muziimba Mosangalala! Nov.

  • Mulungu “Akwanilitse Zofuna Zanu,” July

  • Yehova Atamandike Cifukwa ca Kudzipeleka Kwanu! Apr.

  • Makolo—Thandizani Ana Anu Kupeza ‘Nzelu Zowathandiza Kuti Adzapulumuke,’ Dec.

  • N’cifukwa Ciani Tifunika Kutamanda Yehova? July

  • Pewani Kutengela Maganizo a Dziko, Nov.

  • Kufunafuna Cuma Ceni-ceni, July

  • Tumikilani Yehova ndi Mtima Wathunthu, Mar.

  • Ikani Mtima Wanu pa Cuma Cauzimu, June

  • “Woweluza wa Dziko Lonse” Amacita Cilungamo Nthawi Zonse, Apr.

  • “Mtendele wa Mulungu . . . Umaposa Kuganiza Mozama Kulikonse,” Aug.

  • Dipo—‘Mphatso Yangwilo’ Yocokela kwa Atate, Feb.

  • ‘Zimenezo Uziphunzitse kwa Amuna Okhulupilika,’ Jan.

  • Coonadi ‘Sicibweletsa Mtendele Koma Lupanga,’ Oct.

  • “Mau a Mulungu . . . Ndi Amphamvu,” Sept.

  • “Mau a Mulungu Wathu Adzakhala Mpaka Kalekale,” Sept.

  • Muziyamikila Mphatso Yanu ya Ufulu Wosankha Zocita, Jan.

  • “Khulupilila Yehova Ndipo Cita Zabwino,” Jan.

  • Muzicilikiza Ulamulilo wa Yehova, June

  • Mmene Masomphenya a Zekariya Amakukhudzilani, Oct.

  • “Lilani Ndi Anthu Amene Akulila”, July

  • Kodi Cidzacokapo N’ciani Ufumu wa Mulungu Ukadzabwela? Apr.

  • ‘Muzikwanilitsa Zimene Mwalonjeza,’ Apr.

  • N’ndani Akutsogolela Anthu a Mulungu Masiku Ano? Feb.

  • N’cifukwa Ciani Kudzicepetsa N’kofunikabe? Jan.

  • Kodi Mudzatengelapo Phunzilo pa Zimene Zinalembedwa? Mar.

  • Mukhoza Kukhalabe Wodzicepetsa Ngakhale pa Ciyeso, Jan.

  • Acicepele—“Pitilizani Kukonza Cipulumutso Canu,” Dec.