Mlongoza Nkhani wa Magazini a 2018 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!
Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo
NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA
BAIBO
Kuŵelenga Baibo Kopindulitsa Komanso Kokondweletsa, July
UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU
Muzicitila Cifundo Anthu, July
Cimwemwe—Khalidwe Locokela kwa Mulungu, Feb.
Kukoma Mtima—Kumaonekela M’mawu na M’zocita, Nov.
Kuleza Mtima Kumatanthauza Kupilila Tili na Colinga, Aug.
Mtendele—Kodi Mungaupeze Bwanji? May
“Wolungama Adzakondwela mwa Yehova” Dec.
phamvu ya Moni, June
MBONI ZA YEHOVA
1918—Zimene Zinacitika Zaka 100 Zapitazo, Oct.
Zokolola Zoculuka! (Ukraine), May
Amuna a Paudindo—Tengelani Citsanzo ca Timoteyo, Apr.
Kufesa Mbewu za Ufumu (ku Portugal), Aug.
Anadzipeleka na Mtima Wonse ku Madagascar, Jan.
Anadzipeleka na Mtima Wonse ku Myanmar, July
Akhristu Acikulile—Yehova Amayamikila Kukhulupilika Kwanu, Sept.
Kufalitsa Uthenga Wabwino mwa Nkhani Zapoyela (Ku Ireland), Feb.
Ni Mphatso Yanji Imene Tingam’patse Yehova? (zopeleka), Nov.
MBILI YANGA
Zinthu Zonse N’zotheka kwa Yehova (B. Berdibaev), Feb.
N’nali Wosauka, Koma Lomba N’nalemela (S. Herd), May
N’natonthozedwa pa Mavuto Anga Onse (E. Bazely), June
N’natsimikiza Mtima Kuti Sinidzabwelela M’mbuyo (M. Danyleyko), Aug.
‘Yehova Waticitila Zinthu Zabwino’ (J. Bockaert), Dec.
Yehova Sananigwilitse Mwala (E. Bright), Mar.
Yehova Anan’dalitsa Kwambili Cifukwa ca Zimene N’nasankha (C. Molohan), Oct.
NKHANI ZOSIYANA-SIYANA
Kodi Nthawi Ili Bwanji? (Nthawi za Baibo), Sept.
Akanayanjidwa na Mulungu (Rehobowamu), June
Kodi Mfundo za m’Cilamulo ca Mose Analidi Kuzigwilitsila Nchito Pothetsa Milandu? Jan.
Sitefano anakhalabe wodekha pamene anali kuzunzidwa, Oct.
MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA
Kodi Paulo anatanthauzanji pokamba kuti “anakwatulidwila kumwamba kwacitatu,” ‘n’kukaloŵa m’paradaiso’? (2 Akor. 12:2-4), Dec.
Mwamuna na mkazi osakwatilana akakhala m’nyumba imodzi usiku wonse, kodi angafunike kuwapangila komiti yaciweluzo? July
Kodi Opeleka Zabwino amene Yesu anachula anali ndani? Nov.
N’cifukwa ciani timajambula mtumwi Paulo ali na dazi? Mar.
N’cifukwa ciani n’kosaloleka kuika zofalitsa zathu pa mawebusaiti ena? Apr.
N’cifukwa ciani kamasulidwe ka Salimo 144:12-15 kanasinthidwa? Apr.
NKHANI ZOPHUNZILA
Wamphamvuzonse Koma Woganizila Ena, Sept.
Kodi Mumayesetsa Kuona Zinthu Mmene Yehova Amazionela? Nov.
Ubatizo ni Wofunika kwa Mkhristu Aliyense, Mar.
Khalani Okoma Mtima Komanso Oganizila Ena Monga Yehova, Sept.
“Gula Coonadi Ndipo Usacigulitse,” Nov.
Cilango ni Umboni Wakuti Mulungu Amatikonda, Mar.
Musamaweluze Poona Maonekedwe Akunja, Aug.
Kodi Mudziŵa Bwino Zoona Zake? Aug.
Kodi Mumam’dziŵa Yehova Monga Mmene Nowa, Danieli, na Yobu Anam’dziŵila? Feb.
“Tiyeni Tilimbikitsane, Ndipo Tiwonjezele Kucita Zimenezi,” Apr.
Opatsa Mowoloŵa Manja Amakhala Acimwemwe, Aug.
Acimwemwe ni Anthu Amene Amatumikila “Mulungu Wacimwemwe,” Sept.
“Iye Amapeleka Mphamvu kwa Munthu Wotopa,” Jan.
Muzilemekeza “Cimene Mulungu Wacimanga Pamodzi,” Dec.
“Ngati Zimenezi Mukuzidziŵa, Ndinu Odala Mukamazicita,” Sept.
Tengelani Cikhulupililo ndi Kumvela kwa Nowa, Danieli, na Yobu, Feb.
Tengelani Yehova Mulungu Amene Amapeleka Cilimbikitso, Apr.
“Ndidzayenda M’coonadi Canu,” Nov.
Yehova Amakonda Anthu Amene ‘Amabala Zipatso mwa Kupilila,” May
Pitilizani Kuonetsa Cikondi Cifukwa Cimamangilila, Sept.
M’dziŵeni Mdani Wanu, May
Lolani Malamulo a Mulungu na Mfundo Zake Kuphunzitsa Cikumbumtima Canu, June
“Onetsani Kuwala Kwanu” Kuti Yehova Alemekezeke, June
“Mvelani Malangizo Kuti Mukhale Anzelu,” Mar.
Khalanibe na Mtendele wa mu Mtima Olo Pamene Zinthu Zasintha, Oct.
Tikhale Amodzi, Monga Mmene Yehova na Yesu Alili Amodzi, June
Pitani Patsogolo Monga Munthu Wauzimu! Feb.
“Ufumu Wanga Suli Mbali ya Dziko Lino” June
Makolo, Kodi Mukuthandiza Ana Anu Kupita Patsogolo Kuti Akabatizike? Mar.
Mgwilizano Wokondweletsa pa Cikumbutso, Jan.
Tizidalila Mtsogoleli Wathu—Khristu, Oct.
Muziona Kusiyana Pakati pa Anthu, Jan.
“Tidzaonana M’Paradaiso” Dec.
Tumikilani Yehova, Mulungu wa Ufulu, Apr.
Tizikamba Zoona, Oct.
Kuphunzitsa Coonadi, Oct.
Kucelezana ni Khalidwe Lofunika Kwambili Mar.
Njila Yopezela Ufulu Weni-weni, Apr.
Dalilani Yehova Kuti Mukhalebe na Moyo Nov.
Ndise Anthu a Yehova, July
Kodi Kukhala Munthu Wauzimu Kumatanthauzanji? Feb.
N’cikondi Cotani Cimene Cimabweletsa Cimwemwe Ceni-ceni? Jan.
Kodi Maso Anu Amayang’ana kwa Ndani? July
“Ndani Ali Kumbali ya Yehova?” July
Kodi Mumayendela Maganizo a Ndani? Nov.
Kodi Mumafuna Kukhala Wodziŵika kwa Ndani? July
Kodi N’kumupatsilanji Amene Zonse N’zake? Jan.
Cifukwa Cake ‘Timapitiliza Kubala Zipatso,” May
Muziseŵenza na Yehova Tsiku Lililonse, Aug.
Acicepele Cilimikani Polimbana ndi Mdyelekezi, May
Acicepele, Mungakhale na Umoyo Wacimwemwe, Dec.
Acicepele, Mlengi Wanu Amafuna Kuti Mukhale Acimwemwe, Dec.
Acicepele, Kodi Mumaika Zolinga Zauzimu Patsogolo? Apr.
NSANJA YA MLONDA YOGAŴILA