NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA July 2017

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya August 28-September 24, 2017.

Anadzipeleka na Mtima Wonse—Ku Turkey

Mu 2014, ku Turkey kunacitika nchito yapadela yolalikila. N’cifukwa ciani analinganiza zakuti pacitike nchito imeneyi? Nanga panakhala zotulukapo zanji?

Kufunafuna Cuma Ceni-ceni

Kodi cuma cakuthupi tingaciseŵenzetse bwanji kuti tilimbitse ubwenzi wathu na Yehova?

“Lilani Ndi Anthu Amene Akulila”

Kodi munthu amene wataikilidwa wokondeka wake angapeze bwanji citonthozo? Nanga imwe mungamutonthoze bwanji?

N’cifukwa Ciani Tifunika Kutamanda Yehova?

Salimo 147 imatikumbutsa zifukwa zambili zimene tili nazo zoyamikilila Mlengi wathu.

Mulungu “Akwanilitse Zofuna Zanu”

Acicepele amafunika kusankha mmene adzagwilitsila nchito moyo wawo. Nthawi zina mungacite mantha kupanga zosankha. Koma dziŵani kuti Yehova amadalitsa anthu amene amafuna-funa malangizo ake.

Mungapambane Bwanji Nkhondo Yoteteza Maganizo Anu?

Satana akufalitsa mauthenga abodza pofuna kusokoneza maganizo anu. Kodi mungacite ciani kuti mudziteteze?

Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi

Kodi n’koyenela Mkhristu kukhala na mfuti yodzitetezela kwa anthu ena?