NSANJA YA MLONDA Na. 3 2016 | Munthu Amene Mumakonda Akamwalila

Palibe amene angapewe zotsatilapo imfa. Tingacite ciani ngati wacibale kapena mnzathu wapamtima wamwalila?

NKHANI YA PACIKUTO

Munthu Amene Mumakonda Akamwalila

Kodi munthu angapilile bwanji cisoni? Kodi pali ciyembekezo ciliconse kaamba ka okondedwa athu amene anamwalila?

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Kumva Cisoni n’Kulakwa?

Nanga bwanji ngati anthu ena akuona kuti cisoni canu capitilila malile?

NKHANI YA PACIKUTO

Kupilila Cisoni

Baibulo lili ndi malangizo othandiza.

NKHANI YA PACIKUTO

Kutonthoza Olila

Ngakhale mabwenzi a pamtima angalephele kuzindikila zosoŵa za anthu ofeledwa.

NKHANI YA PACIKUTO

Akufa Adzakhalanso ndi Moyo

Kodi ciyembekezo ca m’Baibulo n’coona?

Kodi Mudziŵa?

Ndani anali atate ake a Yosefe? Kodi m’nthawi za Baibulo kunali nsalu za mitundu yotani?

BAIBO IMASINTHA ANTHU

Ndinaphunzila Kulemekeza Akazi Ndiponso Kudziona Moyenela

Joseph Ehrenbogen anaphunzila Baibulo, cimene cinam’thandiza kusinthilatu umoyo wake.

TENGELANI CIKHULUPILILO CAWO

“Inde Ndipita”

Kuonjezela pa cikhulupililo, Rabeka analinso ndi makhalidwe ena a mtengo wapatali.

Kodi Baibulo Limakamba Ciani?

Kodi n’kulakwa kuchula dzina la Mulungu?