Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mawu Oyamba

Mawu Oyamba

Kodi mumadziŵa bwanji coyenela na cosayenela? Anthu ambili amayendela maganizo awo komanso zimene anaphunzitsidwa. Ena amatengela maganizo a anthu ena popanga zisankho. Kodi nanunso n’zimene mumacita? Nanga mungacite ciyani kuti mupange zisankho zimene zidzathandiza inuyo na banja lanu kukhala na tsogolo labwino?