Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NSANJA YA MLONDA Na. 2 2016 | N’cifukwa Ciani Yesu Anavutika ndi Kufa?

MUGANIZA BWANJI?

Kodi mungapindule ndi mau odziŵika bwino akuti:

“Mulungu anakonda kwambili dziko mwakuti anapeleka Mwana wake wobadwa yekha”? Yohane 3:16.

Nsanja ya Mlonda iyi, ifotokoza mmene mungapindulile cifukwa cakuti Yesu anavutika ndi kutifela.

 

NKHANI YA PACIKUTO

Kodi Zinacitikadi?

N’cinani cimapangitsa Mauthenga Abwino onena za Yesu kukhala oona?

NKHANI YA PACIKUTO

N’cifukwa Ciani Yesu Anavutika Ndi Kufa?

Kodi imfa yake ingakupindulitseni bwanji?

Kodi Akristu Ayenela Kupita ku Tuakacisi Topatulika Kukalambila?

Zipembedzo zikuluzikulu padziko lapansi zili ndi tuakacisi. Kodi kulambila mu tuakacisi tumenetu kuli ndi phindu lililonse?

Kumvela Cenjezo Kumapulumutsa

Maulosi a m’Baibulo amaonetsa kuti cionongeko cili pafupi. Kodi inu mudzawakhulupilila?

Ndani Anagaŵa Baibulo Kuti Likhale ndi Macaputala ndi Mavesi?

N’cifukwa ciani kugaŵa Baibulo mwa njila imeneyo kunakhala kofala?

Kodi Mdyelekezi Ndani?

Kodi muyenela kumuopa?