Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mau Oyamba

Mau Oyamba

MUGANIZA BWANJI?

Kodi mungapindule ndi mau odziŵika bwino akuti:

“Mulungu anakonda kwambili dziko mwakuti anapeleka Mwana wake wobadwa yekha”? Yohane 3:16.

Nsanja ya Mlonda iyi, ifotokoza mmene mungapindulile cifukwa cakuti Yesu anavutika ndi kutifela.