Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Kodi Munadzifunsapo?

Kodi Munadzifunsapo?
  • N’cifukwa ciani padzikoli pali mavuto ambili?

  • Kodi mungacite ciani kuti mupeze nzelu zokuthandizani kupilila mavuto mu umoyo?

  • Kodi Mulungu amasamala za imwe?—1 Petulo 5: 6, 7.

  • Kodi mungacite ciani kuti mudziŵe zambili za Mulungu komanso cifunilo cake?

Anthu ofika mamiliyoni apeza mayankho okhutilitsa pa mafunso amenewa, mwa kuŵelenga Malemba Oyela. Na imwe mungawapeze mayankho.

Ngati mufuna kudziŵa zambili, conde pemphani kabuku kakuti Real Faith—Your Key to a Happy Life, kwa ofalitsa magazini ino ndipo adzakutumizilani mahala, kapena mungakaŵelenge pa intaneti pa www.pr418.com.