NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA February 2016

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzila mlungu wa April 4 mpaka May 1, 2016.

Yehova Anamucha kuti “Bwenzi Langa”

Kodi mungakonde kukhala bwenzi la Yehova? Phunzilani citsanzo ca Abulahamu kuti muone zimene mungacite.

Tengelani Citsanzo ca Mabwenzi Apamtima a Yehova

Kodi n’ciani cinathandiza Rute, Hezekiya, ndi Mariya kukhala pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu?

Khalani Wokhulupilika kwa Yehova

Citsanzo ca Yonatani cingatithandize kukhala wokhulupilika kwa Yehova pa zocitika zinai zovuta.

Tengelani Citsanzo ca Atumiki Okhulupilika a Yehova

Kodi Davide, Yonatani, Natani, ndi Husai anaonetsa bwanji kuti kukhala wokhulupilika kwa Yehova ndiye cinthu coyamba pa umoyo wao?

MBILI YANGA

Yehova Wandidalitsa mu Utumiki Wake

Corwin Robison anatumikila Mulungu mokhulupilika kwa zaka 73, kuphatikizapo zaka zoposa 60 zimene anatumikila pa Beteli ku United States

Pitilizani Kutumikila Yehova Mwacimwemwe

Kusinkhasinkha mfundo zitatu zofunika kungakuthandizeni kukhalabe ndi cimwemwe.