NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA August 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa October 7–November 10, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 31

Zimene Yehova Anacita Kuti Apulumutse Anthu ku Ucimo

Yophunzila mu mlungu wa October 7-13, 2024.

Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga

Kodi kuika munthu cizindikilo kofotokozedwa pa 2 Atesalonika 3:14, kuyenela kucitika na akulu kapena wofalitsa aliyense payekha mumpingo?

NKHANI YOPHUNZILA 32

Yehova Amafuna Kuti Anthu Onse Alape

Yophunzila mu mlungu wa October 14-20, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 33

Mmene Mpingo Umaonetsela Maganizo a Yehova Kwa Munthu Amene Wacita Chimo

Yophunzila mu mlungu wa October 21-27, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 34

Mmene Akulu Amaonetsela Cikondi na Cifundo Kwa Munthu Wocita Chimo

Yophunzila mu mlungu wa October 28–​November 3, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 35

Mmene Akulu Angathandizile Amene Anacotsedwa Mumpingo

Yophunzila mu mlungu wa November 4-10, 2024.

Cidziŵitso Kwa Oŵelenga

M’magazini ino, muli mpambo wa nkhani zophunzila zomwe zidzaonetsa mmene Yehova amaonela aja amene anacita chimo komanso mmene amawathandizila. Tidzaonanso mmene tingatengele khalidwe lake lacikondi na cifundo.