Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mlongoza Nkhani wa Magazini a 2019 a Nsanja Ya Mlonda na Galamuka!

Mlongoza Nkhani wa Magazini a 2019 a Nsanja Ya Mlonda na Galamuka!

Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo

NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA

BAIBO

  • Kuŵelenga Mpukutu Wamakedzana Wakupsa na Moto,” June

UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU

  • Cikhulupililo—Khalidwe Limene Limatithandiza Kukhala Olimba Mwauzimu, Aug.

  • “Muziyamika pa Ciliconse,” Dec.

  • Ubwino—Kodi Tingalikulitse Bwanji Khalidwe Limeneli? Mar.

  • Citsanzo Cabwino pa Nkhani ya Kukhalabe Wacimwemwe (Yohane M’batizi), Aug.

YEHOVA

  • Amacenjeza Anthu Mokwanila? Oct.

  • Amaona Kuti “Ameni” Wanu ni Wofunika,” Mar.

MBONI ZA YEHOVA

  • 1919—Zaka 100 Zapitazo, Oct.

  • Ciwalo Catsopano ca Bungwe Lolamulila (K. Cook, Jr.), Jan.

YESU KHRISTU

  • N’zoona Kuti Ananifela Ine? July

MBILI YANGA

  • Yehova Wanidalitsa Kwambili Kuposa Mmene N’nali Kuyembekezela (M. Tonak), July

  • Coloŵa Cauzimu Cimene N’nalandila Cinanithandiza Kupita Patsogolo (W. Mills), Feb.

  • Tinapeza “Ngale . . . Yamtengo Wapatali” (W. na P. Payne), Apr.

NKHANI ZOSIYANA-SIYANA

  • Ciyambi ca Sunagoge, Feb.

  • Citetezo ku Msampha wa Satana (kutamba zamalisece), June

  • Nchito Imene Mtumiki Woyang’anila Nyumba Anali Kugwila M’nthawi Yakale, Nov.

  • Ulendo Wapanyanja M’nthawi Yamakedzana, Apr.

MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA

  • Kodi ciphunzitso cakuti munthu ali na mzimu umene sumafa cinayambila mu Edeni? (Gen. 3:4), Dec.

  • N’cifukwa ciani mtsikana sanali kukhala na mlandu ngati mwamuna wamugwilila “kuthengo,” olo kuti panalibe mboni ziŵili zotsimikizila colakwaco? (Deut. 22:25-27), Dec.

NKHANI ZOPHUNZILA

  • Lolani Kuti Yehova Akuthandizeni Kukaniza Mizimu Yoipa, Apr.

  • Zimene Zingakuthandizeni Ngati Utumiki Wanu Watha, Aug.

  • Kodi Mumakwanilitsa Mbali Zonse za Utumiki Wanu? Apr.

  • Kodi Mumasamalila Cishango Canu Cacikulu Cacikhulupililo? Nov.

  • Aramagedo ni Nkhani Yokondweletsa! Sept.

  • Limbitsani Ubwenzi Pakati Panu Mapeto Asanafike, Nov.

  • “Bwelani kwa Ine . . . Ndipo Ndidzakutsitsimutsani,” Sept.

  • Tsilizitsani Zimene Munayamba Kucita, Nov.

  • “Usayang’ane Uku ndi Uku Mwamantha, Pakuti Ndine Mulungu Wako,” Jan.

  • Musasoceletsedwe na “Nzelu za M’dzikoli,” May

  • Khalani Wodzipeleka kwa Yehova Yekha, Oct.

  • “Pitani Mukaphunzitse Anthu . . . Kuti Akhale Ophunzila,” July

  • Thandizani Ena Kulimbana na Nkhawa, June

  • Kodi Tingauteteze Bwanji Mtima Wathu? Jan.

  • Mmene Mzimu Woyela Umatithandizila, Nov.

  • Kodi Mumam’dziŵa Bwino Yehova? Dec.

  • Tengelani Citsanzo ca Yesu Kuti Mukhalebe na Mtendele wa Mumtima, Apr.

  • Khalani na Cizoloŵezi Cabwino Coŵelenga, May

  • Yehova Wakonza Zakuti Akupatseni Ufulu, Dec.

  • Yehova Amaona Atumiki Ake Odzicepetsa Kukhala Amtengo Wapatali, Sept.

  • Khalanibe Acangu mu Ndime Ino Yothela ya “Masiku Otsiliza,” Oct.

  • Musaleke Kulambila Yehova pa Nthawi ya Ciletso, July

  • Khalanibe na Mtima Wamphumphu! Feb.

  • Mfundo Zimene Tingaphunzile mu Buku la Levitiko, Nov.

  • Cikondi Canu Cipitilize Kukula, Aug.

  • Mvelani Mawu a Yehova, Mar.

  • Taonani! “Khamu Lalikulu la Anthu,” Sept.

  • ‘Samalani Kuti Wina Angakugwileni Ngati Nyama,’ June

  • Cikondi na Cilungamo M’nthawi ya Aisiraeli, Feb.

  • Cikondi na Cilungamo Mumpingo Wacikhristu, May

  • Cikondi na Cilungamo M’dziko Loipali, May

  • Gubuduzani Maganizo Aliwonse Otsutsana ndi Kudziŵa Mulungu, June

  • Makolo—Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova, Dec.

  • Tamandani Yehova Pakati pa Mpingo, Jan.

  • Konzekelani Cizunzo Pali Pano, July

  • Kulimbikitsa Amene Anacitilidwapo Zolaula, May

  • Kulalikila Anthu Osapembedza Mowafika pa Mtima, July

  • Gonjelani Yehova na Mtima Wonse, Sept.

  • Dalilani Yehova Pamene Muli na Nkhawa, June

  • Yesetsani Kukhala Ofatsa Kuti Mukondweletse Yehova, Feb.

  • Muzimvelela Ena Cifundo, Mar.

  • Onetsani Cifundo Pamene Muli Muulaliki, Mar.

  • Zimene Mungacite Kuti Mudzakhalebe Okhulupilika pa “Cisautso Cacikulu,”Oct.

  • “Pali Nthawi” Yogwila Nchito na Yopumula, Dec.

  • ‘Anthu Okumvelani’ Adzapulumuka, Aug.

  • Cilikizani Coonadi pa Nkhani ya Akufa, Apr.

  • “Sitikubwelela M’mbuyo”! Aug.

  • Zimene Mwambo Wosalila Zambili Umatiphunzitsa Ponena za Mfumu Yathu, Jan.

  • Kodi Kupezeka pa Misonkhano Kumaonetsa Kuti Ndife Anthu Otani? Jan.

  • Cikuniletsa Kubatizika N’ciani? Mar.

  • Kodi Mudzalola Yehova Kukucititsani Kukhala Ndani? Oct.

  • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kuonetsa Kuyamikila? Feb.

NSANJA YA MLONDA YOGAŴILA

  • Kodi Moyo Ukali na Phindu kwa Ine? No. 2

  • Kodi Moyo Ni Uno Cabe Umene Ulipo? No. 3

  • Kodi Mulungu N’ndani? No. 1

GALAMUKA!

  • Kodi Baibo Ingakuthandizeni Kukhala na Umoyo Wabwino? No. 3

  • Zinthu 6 Zimene Ana Afunika Kuphunzila, No. 2

  • Kodi Zidzatheka Kukhala Mwamtendele ndi Motetezeka pa Dzikoli? No. 1