Kalozela wa Nkhani wa Magazini a 2020 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!
Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo
NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA
BAIBO
Kodi zofukula za m’matongwe zimaonetsa bwanji kuti Belisazara wa ku Babulo anali mfumu? Feb.
UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU
Kufatsa—Kodi Khalidweli Limatipindulitsa Bwanji? May
Ika Mtima pa Utumiki Wako! Dec.
Kudziletsa N’kofunika Kuti Tikondweletse Yehova, June
MBONI ZA YEHOVA
1920—Zaka 100 Zapitazo, Oct.
Kulabadila Kulila kwa Lipenga Masiku Ano, June
Madalitso Oculuka kwa Amene Amabwelela ku Dziko la Kwawo, Nov.
MBILI YANGA
“Ife Tilipo! Titumizeni” (J. na M. Bergame), Mar.
Nangocita Zimene N’nayenela Kucita (D. Ridley), July
“Yehova Sananiiŵale” (M. Herman), Nov.
N’napeza Madalitso Ambili Cifukwa Cophunzila kwa Ofalitsa Acitsanzo Cabwino (L. Crépeault), Feb.
NKHANI ZOSIYANA-SIYANA
Umboni woonetsa kuti Aisiraeli anakhalako akapolo ku Iguputo, Mar.
Mafumu Aŵili Olimbana M’nthawi Yamapeto, May
MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA
Kodi makhalidwe ochulidwa pa Agalatiya 5:22, 23 ndiwo okha “amene mzimu woyela umatulutsa”? June
Kodi 1 Akorinto 15:29 Ionetsa kuti Akhristu anali kubatizika cifukwa ca akufa? Dec.
Kodi lemba la Mlaliki 5:8 limakamba cabe za olamulila aumunthu kapena limaphatikizaponso Yehova? Sept.
Kodi Miyambo 24:16 imakamba za munthu amene amagwela m’chimo mobweleza-bweleza? Dec.
Kodi Yesu anakhala liti Mkulu wa Ansembe? Nanga kodi pali kusiyana pakati pa nthawi imene pangano latsopano linayenelezedwa mwalamulo komanso pamene linayamba kugwila nchito? July
Kodi apolisi aciyuda a pa kacisi anali ndani? Nanga anali kugwila nchito yanji? Mar.
NKHANI ZOPHUNZILA
Citani Zinthu Mwanzelu Panthawi ya Mtendele, Sept.
Kuukila kwa Mdani Wocokela Kumpoto! Apr.
Kodi Mukuyembekezela “Mzinda Wokhala Ndi Maziko Eni-eni”? Aug.
Kodi Ndimwe Wokonzeka Kukhala Msodzi wa Anthu? Sept.
Kodi Ndimwe Wokonzeka Kubatizika? Mar.
Kodi Mumakhulupililadi Kuti Muli na Coonadi? July
“Dzanja Lako Lisapume,” Sept.
“Musamadziganizile Kuposa Mmene Muyenela Kudziganizila,” July
Kodi Mumayamikila Mphatso Zimene Mulungu Anakupatsani? May
Muziwathandiza Alongo Mumpingo, Sept.
‘Pitani Mukaphunzitse Anthu Kuti Akhale Ophunzila Anga,’ Jan.
‘Sungani Bwino Cimene Cinaikidwa M’manja Mwanu,’ Sept.
“Kodi Akufa Adzaukitsidwa Motani?” Dec.
Kodi Mumawaona Bwanji Anthu a mu Gawo Lanu? Apr.
Mmene Tingatsogozele Phunzilo la Baibo Lotsogolela Munthu ku Ubatizo—Gawo 1, Oct.
Mmene Tingatsogozele Phunzilo la Baibo Lotsogolela Munthu ku Ubatizo—Gawo 2, Oct.
Mmene Tingathandizile Ena Kusunga Malamulo a Khristu, Nov.
Mmene Tingagonjetsele Zolefula, Dec.
“Nakuchani Mabwenzi,” Apr.
“Inetu Ndidzafunafuna Nkhosa Zanga,” June
Yehova Akutsogolela Gulu Lake, Oct.
Atate Wathu Yehova, Amatikonda Kwambili, Feb.
Yehova Amapulumutsa Anthu Olefuka Mtima, Dec.
Yehova Mulungu Wathu Amationa Kuti Ndife Ofunika! Jan.
Pitilizani Kuyenda m’Coonadi, July
Lolani Kuti Yehova Akutonthozeni, Feb.
“Dzina Lanu Liyeletsedwe,” June
Amvetseleni, Adziŵeni Bwino, Aonetseni Cifundo, Apr.
Yang’anani Kutsogolo, Nov.
Kukonda Yehova na Kum’yamikila Kudzakusonkhezelani Kubatizika, Mar.
Muzikondana Kwambili, Mar.
Yesetsani Kulimbikitsa Mtendele mwa Kuthetsa Kaduka, Feb.
Lemekezani Wina Aliyense mu Mpingo, Aug.
“Bwelelani kwa Ine,” June
“Nathamanga Panjilayo Mpaka pa Mapeto,” Apr.
Onetsani Kuti Mumayamikila Cuma Cosaoneka, May
Limbani Mtima—Yehova Ndiye Mthandizi Wanu, Nov.
“Mfumu ya Kumpoto” M’nthawi Yamapeto, May
Akufa Adzauka Ndithu—Sitikaika Konse! Dec.
Ciukililo Cimaonetsa Kuti Mulungu ni Wacikondi, Wanzelu, Komanso Woleza Mtima, Aug.
‘Mzimu Umacitila Umboni Limodzi Ndi Mzimu Wathu,’ Jan.
“Ndipatseni Mtima Wosagawanika Kuti Ndiope Dzina Lanu,” June
Muziyenda Modzicepetsa na Mulungu Wanu, Aug.
Timam’konda Kwambili Atate Wathu Yehova, Feb.
Tipita Nanu Limodzi, Jan.
“Pamene Ndili Wofooka, M’pamene Ndimakhala Wamphamvu,” July
Kodi Nthawi Yoyenela Kukamba ni Iti? Mar.
Kodi “Mfumu ya Kumpoto” Ndani Masiku Ano? May
Kodi Ana Anu Adzatumikilabe Yehova Akakula? Oct.
Kodi Mudzakhalabe Okonzeka Kusintha? Nov.
Mungathe Kulimbikitsa Ena Kwambili, Jan.
Na Imwe Muli na Malo mu Mpingo wa Yehova! Aug.
NSANJA YA MLONDA YOGAŴILA