Mlozela Nkhani wa Magazini a 2022 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!
Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo
NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA
KODI MUDZIŴA?
Kodi anthu ochulidwa m’Baibo anali kudziŵa bwanji poyambila caka kapena mwezi? June
Kodi Aroma anali kulola munthu wopacikidwa pa mtengo, monga Yesu, kuti mtembo wake uikidwe m’manda? June
Kodi Moredekai analikodi? Nov.
N’cifukwa ciani Aisiraeli kalelo anali kupeleka malipilo a ukwati? Feb.
N’cifukwa ciani njiŵa komanso ana a nkhunda zinali kulandilidwa monga nsembe? Feb.
MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA
Kodi Baibo imati ciyani pa nkhani ya kucita malumbilo? Apr.
Kodi Davide ‘anamvelela bwanji cifundo’ Mefiboseti, koma pambuyo pake anapeleka Mefiboseti kuti akaphedwe? (2 Sam. 21:7-9), Mar.
Kodi Davide anali kuganiza kuti sadzamwalila polemba kuti adzatamanda dzina la Mulungu “mpaka muyaya”? (Sal. 61:8), Dec.
Kodi mtumwi Paulo anatanthauza ciyani pamene anati iye ni “khanda lobadwa masiku asanakwane”? (1 Akor. 15:8), Sept.
Kodi Yesu anatanthauza ciyani pokamba kuti: “Musaganize kuti ndinabweletsa mtendele”? (Mat. 10:34, 35), July
Mmene mpingo uyenela kuonela ukwati wakalewo ndiponso ukwati watsopanowo ngati Mkhristu si womasuka mwa Malemba, Apr.
Ndani adzaukitsidwa pano padziko lapansi? Nanga ciukitso cawo cidzakhala cotani? Sept.
MBILI YANGA
“N’nakwanilitsa Colinga Canga Cotumikila Yehova” (D. van Marl), Nov.
N’nalola Yehova Kunitsogolela Njila (K. Eaton), July
N’napeza Cinthu Cabwino Kuposa Kukhala Dokotala (R. Ruhlmann), Feb.
Nakhala Nikusangalala Kuphunzila za Yehova na Kuphunzitsako Ena (L. Weaver, Jr.), Sept.
MBONI ZA YEHOVA
1922—Zaka 100 Zapitazo, Oct.
NKHANI ZOPHUNZILA
Anthu a Yehova Amakonda Cilungamo, Aug.
Buku la Chivumbulutso—Cimene Cidzacitikila Adani a Mulungu, May
Buku la Chivumbulutso—Mmene Likukhudzila Tsogolo Lanu, May
Buku la Chivumbulutso—Mmene Limakukhudzilani, May
Cifukwa Cake Timapezeka pa Cikumbutso, Jan.
Cikondi ca Yehova Cimatithandiza Kugonjetsa Mantha, June
Inu Acicepele—Pitanibe Patsogolo Pambuyo pa Ubatizo, Aug.
Inu Akulu—Pitilizani Kutsanzila Mtumwi Paulo, Mar.
Inu Anakubala—Phunzilani ku Citsanzo ca Yunike, Apr.
Inu Makolo—Thandizani Ana Anu Kukonda Yehova, May
Khalanibe Oganiza Bwino Kukhulupilika Kwanu Kukayesedwa, Nov.
Kodi Dzina Lanu Lilimo “M’buku la Moyo”? Sept.
Kodi Mumakhulupilila Mmene Yehova Amacitila Zinthu? Feb.
Kodi Mumatha Kuona Zimene Zekariya Anaona? Mar.
Kodi Ndinu “Citsanzo . . . M’kalankhulidwe”? Apr.
Kodi Uphungu Wanu ‘Umasangalatsa Mtima’? Feb.
Kodi Yehova Amatithandiza Bwanji Kupilila Mwacimwemwe? Nov.
Kulambila Koona Kudzawonjezela Cimwemwe Canu, Mar.
‘Kuthandiza Anthu Ambili Kukhala Olungama,’ Sept.
Maso a Yehova Ali pa Anthu Ake, Aug.
Mmene Mungadziikile Zolinga Zauzimu na Kuzikwanilitsa, Apr.
Mmene Yehova Amatithandizila Kugwila Nchito Yolalikila, Nov.
Mukhoza Kucipeza Cimwemwe Ceniceni, Oct.
Musalole Ciliconse Kukulekanitsani na Yehova, Nov.
“Muzigwilitsa Nchito Bwino Nthawi Yanu,” Jan.
‘Mvela Mawu a Anthu Anzelu,’ Feb.
N’zotheka Kudzakhala na Moyo Kwamuyaya, Dec.
N’zotheka Kuti Muziwadalila Abale Anu, Sept.
N’zotheka ‘Kuvula Umunthu Wakale,’ Mar.
Nzelu Yeniyeni Imafuula, Oct.
Nzelu Zothandiza pa Umoyo Wathu, May
“Odala ndi Anthu Osalakwitsa Kanthu” kwa Yehova, Oct.
“Ofuna-funa Yehova Sadzasoŵa Ciliconse Cabwino,” Jan.
Onetsani Kuti Ndinu Wodalilika, Sept.
Pezani Cimwemwe Popatsa Yehova Zabwino Zimene Mungathe Pacanu, Apr.
Pezani Mtendele pa Nthawi ya Mavuto, Dec.
Phunzilani Kwa Mng’ono Wake wa Yesu, Jan.
Pitilizani “Kulimbikitsana,” Aug.
Pitilizani Kulimbitsa Ciyembekezo Canu, Oct.
Pitilizani Kuvala “Umunthu Watsopano” Pambuyo pa Ubatizo, Mar.
Tengelani Citsanzo ca Yesu Cotumikila Ena, Feb.
Thandizani Ena Kupilila pa Nthawi Zovuta, Dec.
Tiyeni Tim’thandizile Yesu Monga Wotiyang’anila, July
Tiziyamikila Mwayi Wathu wa Pemphelo, July
“Udzakhala Ndi Ine m’Paradaiso,” Dec.
Ufumu wa Mulungu Ukulamulila! July
Ulosi Wamakedzana Umene Umakukhudzani, July
Yehova Amadalitsa Amene Amakhululukila Anzawo, June
Yehova Ni Wokonzeka Kukhululuka, June
“Yembekezela Yehova,” June
‘Yendanibe M’coonadi,’ Aug.
Yesu Anagwetsa Misozi—Tiphunzilapo Ciani? Jan.
UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU
NSANJA YA OLONDA YOGAŴILA
Kodi N’zotheka Kuthetsa Chidani? (Chichewa) Na. 1
GALAMUKANI!
Kodi Mungatani Kuti Mupirire Mavuto a M’Dzikoli? (Chichewa) Na. 1