Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mlozela Nkhani wa Magazini a 2023 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Mlozela Nkhani wa Magazini a 2023 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo

NSANJA YA MLONDA YOPHUNZILA

UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHRISTU

  • Yendelani Malangizo a Mulungu pa Nkhani ya Moŵa, Dec.

  • Anaona Cikondi Ceniceni, Feb.

  • Ngati Mnzanu wa mu Ukwati Amaonelela Zamalisece, Aug.

KODI MUDZIŴA?

  • Kodi nchelwa zimene anapeza pa matongwe a Babulo wakale komanso mmene anaziumbila, zionetsa bwanji kuti Baibo ni yolondola? July

MBONI ZA YEHOVA

  • 1923—Zaka 100 Zapitazo, Oct.

  • Muzimvela Anthu Onse Cifundo, Dec.

  • Hulda Anakwanilitsa Colinga Cake, Nov.

MBILI YANGA

  • Napeza Citetezo Ceniceni Podalila Yehova (I. Itajobi), Nov.

  • Nakhala Nikuona Cikhulupililo ca Anthu a Yehova (R. Landis), Feb.

  • Yehova Watidabwitsa na Kutiphunzitsa Pom’tumikila (R. Kesk), June

  • Kuonetsa Ena Cidwi Kumabweletsa Madalitso Okhalitsa (R. Reid), July

MAFUNSO OCOKELA KWA OŴELENGA

  • Yesu atabadwa, n’cifukwa ciyani Yosefe na Mariya anakhalabe ku Betelehemu m’malo mobwelela kwawo ku Nazareti? June

  • Kodi Aisiraeli analiko na zakudya zina kupatulapo mana na zinzili m’cipululu? Oct.

  • Kodi nkhani yakuti “Dzina Lanu Liyeletsedwe” mu Nsanja ya Mlonda ya June 2020, inaunika motani kamvedwe kathu pa nkhani yokhudza dzina la Mulungu na ulamulilo wake? Aug.

  • N’cifukwa ciyani munthu wochedwa “Uje” ananena kuti ‘akanawononga’ colowa cake akanakwatila Rute? (Rute 4:​1, 6), Mar.

NKHANI ZOPHUNZILA

  • Kodi Mwacikonzekela Cisautso Cacikulu? July

  • Kodi Ndinu ‘Wokonzeka Kumvela’? Oct.

  • Kodi Ubatizo Mungaukonzekele Motani? Mar.

  • Khalani Otsimikiza Kuti ‘Mawu a Mulungu Ndi Coonadi’, Jan.

  • “Khalani Olimba, Osasunthika,” July

  • “Sandulikani Mwa Kusintha Maganizo Anu,” Jan.

  • “Mwakutelo, Onse Adzadziŵa Kuti Ndinu Ophunzila Anga,” Mar.

  • Nyamulani Zofunikila Zokhazo, Tayani Zotsalazo, Aug.

  • Yamikilani Mphatso ya Mulungu ya Moyo, Feb.

  • Yamikilani Mwayi Wanu Wolambila Yehova M’kacisi Wake Wauzimu, Oct.

  • Pitilizani Kupindula na Mantha Aumulungu, June

  • Khalanibe Oleza Mtima, Aug.

  • Inu Akulu—Tengelani Citsanzo ca Gidiyoni, June

  • Tizilimbikitsana pa Misonkhano ya Mpingo, Apr.

  • Ciyembekezo Cathu N’cosagwilitsa Mwala, Dec.

  • Yesetsani Kumvetsa Milingo Yonse ya Mawu a Mulungu, Oct.

  • Cikhulupililo na Nchito Zake Zimapangitsa Munthu Kukhala Wolungama, Dec.

  • Zimene Mungacite Kuti Muzipindula Kwambili Poŵelenga Baibo, Feb.

  • Mulungu ‘Adzakupatsani Mphamvu’—Motani? Oct.

  • Tingalimbitse Motani Cikhulupililo Cathu pa Lonjezo la Yehova la Dziko Latsopano? Apr.

  • Mmene Yehova Amayankhila Mapemphelo Athu, May

  • Yehova Akutitsimikizila za Lonjezo la Paradaiso-Motani? Nov.

  • Mmene Tingalimbikitsile Cikondi Cathu pa Ena, Nov.

  • Khalani Ololela Potengela Yehova, July

  • Kuwongolela Mapemphelo Athu, May

  • Yehova Amadalitsa Kuyesetsa Kwathu Kuti Ticite Cikumbutso, Jan.

  • Yehova Akukuthandizani Kupambana Mayeso, Jan.

  • Yehova Adzakuthandizani pa Zakugwa Mwadzidzidzi, Apr.

  • Muzikulabe m’Cikondi Canu, July

  • Khalanibe Okonzeka Tsiku la Yehova, June

  • Musalole “Lawi la Ya” Kuzima, May

  • Yendanibe pa “Msewu wa Ciyelo,” May

  • “Khalanibe Oganiza Bwino Ndipo Khalani Maso!” Feb.

  • Phunzilani ku Maulosi a m’Baibo, Aug.

  • Tengelani Citsanzo ca Danieli, Aug.

  • Phunzilani Zambili za Yehova Poyang’ana Cilengedwe Cake, Mar.

  • Zimene Tingaphunzile M’makalata Aŵili a Petulo, Sept.

  • Khalani Wamphamvu Pokhala Wofatsa, Sept.

  • Limbikilani Monga Anacitila Petulo, Sept.

  • Muzidalila Yehova Mmene Samisoni Anacitila, Sept.

  • ‘Cikondi Cimene Khristu Ali Naco Cimatilimbikitsa,’ Jan.

  • Gwilitsani Nchito Zacilengedwe Pophunzitsa Ana Anu za Yehova, Mar.

  • Tiphunzilapo Ciyani pa Zozizwitsa za Yesu? Apr.

  • Kodi Baibo Imatiphunzitsanji za Mwiniwake wa Mawu a m’Bukulo? Feb.

  • N’cifukwa Ciyani Muyenela Kubatizika? Mar.

  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kumuopa Yehova? June

  • Kodi Yehova Adzayankha Mapemphelo Anga? Nov.

  • N’zotheka Kuzikwanilitsa Zolinga Zanu Zauzimu, May

  • Mungakhalebe na Cidalilo mu Nthawi Zovuta, Nov.

  • Inu Abale Acinyamata—Khalani Amuna Okhwima Mwauzimu, Dec.

  • Acinyamata—Kodi Mudzakhala na Tsogolo Lotani? Sept.

  • Inu Alongo Acitsikana—Khalani Akazi Okhwima Mwauzimu, Dec.

  • “Mlongo Wako Adzauka”! Apr.

MFUNDO ZOTHANDIZA PA KUŴELENGA KWANU

  • Kodi Mumapindula Nako Kufotokozela Vesi la m’Baibo Kopezeka mu Buku Lofufuzila Nkhani? Apr.

  • Zida Zophunzitsila Ana (jw.org), Sept.

  • Kupeza Nkhani Zimene Zinaikidwapo pa Webusaiti (jw.org), Feb.

  • Pezani Cuma ca Kuuzimu Cokhudza Yehova (Watch Tower Publication Index kapena Buku Lofufuzila Nkhani) Aug.

  • Mmene Mungapezele Masinthidwe pa Kamvedwe Kathu Katsopano (Watch Tower Publication Index kapena Buku Lofufuzila Nkhani), Oct.

  • Loŵezani pa mtima “Nyimbo Zauzimu” (jw.org) Nov.

  • Kodi Mumakonda Kuŵelenga Nkhani Zakuti “Mbili Yanga”? Jan.

  • Malifalensi Opezeka mu Watchtower LAIBULALI YA PA INTANETI, May

  • Nkhani Zimene Si Zophunzila mu Nsanja ya Mlonda (JW Library®), June

  • Ikani Patsogolo Zinthu Zofunika Kwambili, July

  • Kugwilitsa Nchito Bwino Mbali Yakuti “N’ciani Catsopano?” (JW Library® na jw.org), Mar.

NSANJA YA MLONDA YOGAŴILA

  • Baibo Ingathandize Odwala Matenda a Maganizo, Na. 1

GALAMUKA!

  • Kodi Dziko Lapansi Lidzapulumuka? Zifukwa Zokhalila na Ciyembekezo, Na. 1