NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa February 3–March 2, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 48

Kuculukitsa Mikate Mozizwitsa

Yophunzila mu mlungu wa February 3-9, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 49

N’zotheka Kwa Inu Kukakhala na Moyo Wosatha—Motani?

Yophunzila mu mlungu wa February 10-16, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 50

Makolo—Thandizani Ana Anu Kulimbitsa Cikhulupililo Cawo

Yophunzila mu mlungu wa February 17-23, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 51

Misozi Yanu Ni Yamtengo Wapatali kwa Yehova

Yophunzila mu mlungu wa February 24–March 2, 2025.

MBILI YANGA

Sin’nasiye Kuphunzila

M’bale Joel Adams akufotokoza zimene zamuthandiza kupilila mwacimwemwe potumikila Yehova kwa zaka zoposa 80.

Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga

Kodi “angelo ocita kusankhidwa” ochulidwa pa 1 Timoteyo 5:21 ndani?

Kodi Mukukumbukila?

Kodi munaŵelenga mosamala magazini a caka cino a Nsanja ya Mlonda? Onani zimene mungakumbukile.

Anthu Okhulupilika Amasunga Malonjezo Awo

Ni maphunzilo otani amene tingatengepo pa nkhani ya Yefita na mwana wake wamkazi?