NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA February 2024
Maganizo ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa April 8–May 5, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 5
“Sindidzakusiyani Kapena Kukutayani Ngakhale Pang’ono”!
Yophunzila mu mlungu wa April 8-14, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 8
Musaleke Kutsatila Citsogozo ca Yehova
Yophunzila mu mlungu wa April 29–May 5, 2024.
Pezani Cimwemwe Poyembekezela Yehova Moleza Mtima
Anthu ambili amalefulidwa na dongosolo lino la zinthu pomwe akuyembekezela kuti Yehova acitepo kanthu pa nthawi yake. N’ciyani cingatipeputsileko zinthu pamene tikuyembekezela, na kutithandiza kupeza cimwemwe pamene ticita zimenezi?
Ziwalo Ziŵili Zatsopano za Bungwe Lolamulila
Pa Citatu, January 18, 2023, panapelekewa cilengezo cakuti M’bale Gage Fleegle na M’bale Jeffrey Winder aikidwa kuti azitumikila monga ziwalo za Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova.
Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga
Kodi Baibo imatiululila ciyani za mphamvu za Yehova zokwanitsa kunenelatu zamtsogolo?
Kodi Mudziŵa?
Ganizilani zifukwa zitatu zimene ziyenela kuti zinapangitsa olemba Baibo kucita zimenezi.
MFUNDO YOTHANDIZA PA KUŴELENGA KWANU