NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA February 2025

Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila mu mlungu wa April 14–​May 4, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 6

Cifukwa Cake Timayamikila Kuti Yehova Amatikhululukila

Yophunzila mu mlungu wa April 14-20, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 7

Mmene Kukhululuka kwa Yehova Kumatipindulila

Yophunzila mu mlungu wa April 21-27, 2025.

NKHANI YOPHUNZILA 8

Tingatengele Bwanji Kukhululuka kwa Yehova?

Yophunzila mu mlungu wa April 28–​May 4, 2025.

MBILI YANGA

“Sindinakhalepo Ndekhandekha”

Onani cifukwa cake Angelito Balboa amakhulupilila kuti Yehova anali naye nthawi zonse, ngakhale pamene anakumana mayeso ovuta.

Pewani Mzimu Wodzikonda Umene Wafala Masiku Ano

Anthu ambili masiku ano amaganiza kuti ayenela kupatsidwa maudindo apadela, komanso kucitilidwa zinthu m’njila yapadela kuposa ena. Onankoni zina mwa mfundo za m’Baibulo zimene zingatithandize kupewa kaganizidwe ka conco.

Mmene Mungakhalile Bwenzi Lenileni

Baibulo limaonetsa kuti kukhala ndi mabwenzi enieni m‘nthawi ya mavuto n’kofunika kwambili.

Funso Losavuta Limene Lingakhale ndi Zotulukapo Zabwino

Monga zinalili ndi Mary, inunso mukhoza kuyambitsa maphunzilo a Baibulo mwa kufunsa funso losavuta.

Onetsani Kulimba Mtima Mukapanikizika

Kodi tingaphunzileponji pa kulimba mtima komwe anaonetsa Yeremiya ndi Ebedi-meleki?