NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA October 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa December 9, 2024–​January 5, 2025.

1924—Zaka 100 Zapitazo

M’caka ca 1924, Ophunzila Baibo anagwilitsila nchito njila zatsopano kuti apitilize kulalikila uthenga wabwino molimba mtima.

NKHANI YOPHUNZILA 40

Yehova “Amacilitsa Anthu Osweka Mtima”

Yophunzila mu mlungu wa December 9-15, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 41

Zimene Yesu Anacita M’masiku Ake 40 Othela Padziko Lapansi

Yophunzila mu mlungu wa December 16-22, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 42

Muzionetsa kuti Mumayamikila “Mphatso za Amuna”

Yophunzila mu mlungu wa December 23-29, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 43

Mmene Tingathetsele Zikaiko Zathu

Yophunzila mu mlungu wa December 30, 2024–​January 5, 2025.

Kodi Mudziŵa?

Kodi nyimbo zinali zofunika motani kwa Aisiraeli akale?

Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga

Kodi khonde la kacisi wa Solomo linali lalitali motani?

Muzibwelelamo mu Mfundo Zikulu-zikulu

Kodi mumavutika kukumbukila zimene mwacoka kuŵelenga? N’ciyani cingakuthandizeni kuti muzikumbukila zimene mwaŵelenga?