NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA September 2016

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila mlungu wa October 24 mpaka November 27, 2016.

“Manja Anu Asakhale Olefuka”

Kodi Yehova amalimbikitsa ndi kuthandiza bwanji atumiki ake? Nanga inu mungacite bwanji zimenezi kwa ena?

Cilimikani pa Kulimbana Kuti Mupeze Madalitso a Yehova

Atumiki a Mulungu amakumana ndi mayeselo ambili pamene acilimika kuti apeze madalitso ake. Koma n’zotheka iwo kupambana

Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi

Kodi “mau a Mulungu” amene lemba la Aheberi 4:12 limakamba kuti ndi “amoyo ndi amphamvu” n’ciani?

Kuteteza Uthenga Wabwino Pamaso pa Akulu-akulu a Boma

Tingaphunzile zambili tikaona mmene Paulo anagwilitsila nchito malamulo a boma kuti adziteteze.

Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu?

Mfundo za m’Baibulo zingatithandize.

Ubwino Wotsatila Malangizo a Yehova

Mboni za m’dziko la Poland ndi Fiji zinasankha mwanzelu.

Wacicepele, Limbitsa Cikhulupililo Cako

Kodi nthawi zina umakhumbilako zimene ambili amakhulupilila, monga cisanduliko m’malo mwa cilengedwe? Ngati n’conco, magazini ino idzakuthandiza.

Makolo, Thandizani Ana Anu Kukhala na Cikhulupililo

Kodi nthawi zina mumaona kuti simungakwanitse? Pali masitepu anayi amene angakuthandizeni.