NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA September 2018

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya October 29-December 2, 2018

“Ngati Zimenezi Mukuzidziŵa, Ndinu Odala Mukamazicita”

Tingacite ciani kuti tikhalebe odzicepetsa? Nanga n’cifukwa ciani kucita zimenezo n’kofunika?

Akhristu Acikulile—Yehova Amayamikila Kukhulupilika Kwanu

Kodi abale acikulile aonetsa bwanji kudzicepetsa masiku ano?

Pitilizani Kuonetsa Cikondi Cifukwa Cimamangilila

Phunzilani mmene tingalimbikitsilane m’masiku otsiliza ovuta ano.

Acimwemwe ni Anthu Amene Amatumikila “Mulungu Wacimwemwe”

N’ciani cingatithandize kukhalabe acimwemwe olo timakumana na mavuto?

Kodi Nthawi Ili Bwanji?

Kodi anthu anali kuchula bwanji nthawi m’masiku akale?

Wamphamvuzonse Koma Woganizila Ena

Kodi Yehova amapeleka bwanji citsanzo cabwino pa nkhani ya kuganizila ena?

Khalani Okoma Mtima Komanso Oganizila Ena Monga Yehova

Phunzilani njila zosiyana-siyana zoonetsela kuti timaganizila ena m’banja, mu mpingo, na mu ulaliki.