Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mlozela Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Mlonda a 2014

Mlozela Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Mlonda a 2014

Tasonyeza deti la magazini imene muli nkhani

BAIBULO

  • Linalembedwa Bwanji? 2/1

  • Ndi Maudi a Mulungu? 2/1

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

  • Kulikonse kumene ndinali kupita, ndinali kukhala ndi mfuti yanga (A. Lugarà), 7/1

  • Ndinali wodzikonda (C. Bauer),—November-December

    • Ndinamenya nkhondo yandekha kuti ndithetse kupanda cilungamo ndi nkhanza (A. Touma),—September-October

    NKHANI ZOPHUNZILA

  • “Anthu Amene Mulungu Wao Ndi Yehova,” 11/15

  • Anthu a Yehova “Aleke Kucita Zosalungama,” 7/15

  • Cifukwa Cake Tifunika Kukhala Oyela, 11/15

  • Gwilitsilani Nchito Mau a Mulungu—Ndi Amoyo, 8/15

  • “Ikani Maganizo Anu pa Zinthu Zakumwamba,” 10/15

  • Imfa, Mdani Wotsilizila, Idzaonongedwa, 9/15

  • “Inu Ndinu Mboni Zanga,” 7/15

  • Khalani ndi Cikhulupililo Cosagwedela mu Ufumu, 10/15

  • Khalani ndi Mzimu Wodzimana, 3/1

  • Kodi Kuukitsidwa kwa Yesu Kumatanthauza Ciani kwa Ife? 11/15

  • Kodi Mumakhulupilila Kuti Muli ndi Coonadi? N’cifukwa Ciani? 9/15

  • Kodi ‘Mumamvetsa Tanthauzo la Malemba’? 12/15

  • Kodi Mumaona “Wosaonekayo”? 4/1

  • Kodi Mumaona Zofooka za Anthu Mmene Yehova Amazionela? 6/1

  • Kodi Mumayamikila Cisamalilo Cacikondi ca Yehova? 4/1

  • Kodi Mumayamikila Zimene Munalandila? 12/15

  • Kodi Mumayendela Limodzi ndi Gulu la Yehova? 5/1

  • NKHANI ZOSIYANASIYANA

    • Anapilila Zinthu Zopanda Cilungamo, (Eliya), 2/1

    • Cipembedzo Coona,—September-October

    • Colinga ca Dziko Lapansi, 6/1

    • Gulaye pomenya nkhondo m’nthawi zakale, 5/1

    • Kodi Anthu Adzaononga Dziko Lapansi Kothelatu?—November-December

    • Kodi Cilamulo ca Mulungu kwa Aisiraeli Cinali Colungama ndi Cosakondela?—November-December

    • Kodi Imfa Ndi Mapeto a Zonse? 1/1

    • Kodi oyenda panyanja akalekale anali kupanga bwanji ngalawa zao kuti madzi asaziloŵa?—July-August

    • Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulila?—November-December 11/1

    • Mgwilizano wa Zipembedzo, 3/1

    • Mkate Wamoyo, 6/1

    • Mmene Mungalangile Ana Anu—July-August

    • Mulungu Amakuona Bwanji Kukoka Fodya? 6/1

    • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela Kuti Ufumu Ubwele?—November-December

    • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela? Tizipemphela Bwanji?—July-August

    • N’cifukwa Ciani Zigaŵenga Anali Kuzithyola Miyendo Pozipha? 5/1

    • N’cifukwa Ciani Zoipa Zimacitikila Anthu Abwino?—July-August

    • Ndani Amadziŵa Zamtsogolo? 5/1

    • Ndani Kwenikweni Akulamulila Dzikoli? 5/1

    • Nkhondo Imene Inasintha Zinthu Padziko (Nkhondo yoyamba ya padziko lonse), 2/1

    • Pali Ciyembekezo Cotani Ponena za Makolo Akale? 6/1

    • ‘Tamvelani Maloto Awa’ (Yosefe),—September-October

    YEHOVA

    YESU KRISTU

  • Adzacita ciani mtsogolo? 4/1

  • Akucita ciani tsopano? 4/1

  • Cocitika Cimene Simuyenela Kuphonya (Cikumbutso), 3/1

    • Timapindula bwanji ndi imfa ya Yesu? 3/1

    • Tiyenela kukumbukila bwanji imfa ya Yesu? 3/1