NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA November 2015

M’magaziniyi muli nkhani zophunzila za mlungu wa December 28, 2015, mpaka January 31, 2016.

Phunzitsani Ana Anu Kutumikila Yehova

Makhalidwe atatu amene Yesu anasonyeza pophunzitsa angakuthandizeni kuphunzitsa ana anu mogwila mtima.

Phunzitsani Ana Anu Acinyamata Kutumikila Yehova

Kodi mungathandize bwanji ana anu acinyamata kukula mwakuuzimu?

Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi

N’ciani cimene cimaonetsa kuti mzinda wa Yeriko unaonongedwa m’kanthawi kocepa?

Yehova Ndi Mulungu Wacikondi

Kodi Yehova waonetsa bwanji kuti amakonda anthu?

Kodi ‘Mumakonda Anzanu Mmene Mumadzikondela’?

Mungatsatile lamulo la Yesu m’cikwati, mumpingo, ndi muulaliki.

Zaka 100 za Ulamulilo wa Ufumu wa Mulungu

Ndi zinthu zitatu ziti zimene zatithandiza kugwila bwino nchito yolalikila za Ufumu wa Mulungu?