NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2015

Magaziniyi ili ndi nkhani zophunzila za mlungu wa February 1 mpaka 28, 2016.

Yehova Mulungu Amakonda Kukamba ndi Anthu

Mulungu amagwilitsila nchito zinenelo zosiyanasiyana pokambilana ndi anthu. Zimenezi zimatiphunzitsa mfundo yofunika kwambili ya coonadi.

Baibulo Lomasulidwa Bwino Kwambili

A Komiti Yomasulila Baibulo la Dziko Latsopano anatsatila mfundo zitatu zofunika kwambili

Muziyamikila Kuolowa Manja kwa Yehova

Baibulo limafotokoza zolinga zimene tiyenela kukhala nazo pamene tigwilitsila nchito nthawi yathu, mphamvu zathu, ndi cuma cathu pocilikiza zinthu za Ufumu. Ifotokozanso zolinga zimene tiyenela kupewa pamene ticita zimenezi.

Gwilitsilani Nchito Bwino Lilime Lanu

Kodi citsanzo ca Yesu cingakuthandizeni bwanji kudziŵa nthawi yoyenela kukamba, zimene muyenela kukamba, ndi mmene muyenela kukambila?

Yehova Adzakucilikizani

Kodi matenda tiyenela kuwaona bwanji? Nanga tiyenela kucita ciani tikadwala?

MBILI YANGA

Ndili pa Mtendele ndi Mulungu Komanso ndi Amai

Pamene Michiyo Kumagai analeka kulambila mizimu ya makolo akale, amai ake analeka kugwilizana naye? Kodi Michiyo anacita ciani kuti ayambenso kugwilizana nao?