NSANJA YA MLONDA Na. 1 2016 | N’zotheka Kumvetsetsa Baibulo

Kodi munadzifunsapo kuti, ‘N’cifukwa ciani Baibulo ndi lovuta kumvetsetsa?’

NKHANI YA PACIKUTO

Why Understand the Bible?

Many respect this sacred book without realizing how it can benefit them.

NKHANI YA PACIKUTO

Buku Losavuta Kumvetsetsa

Mfundo zinai zimene zionetsa kuti anthu amitundu yonse akhoza kumvetsetsa Baibulo.

NKHANI YA PACIKUTO

Pemphani Thandizo Kuti Mumvetsetse Baibulo

Ngati n’zotheka kumvetsetsa Baibulo, n’cifukwa ciani mufunika thandizo kuti mulimvetsetse?

Cinyengo, Kodi Cidzatha?

Kodi anthu onyenga akuthandizani kusiya zandale, cipembedzo, kapena zamalonda?

Kodi Mudziŵa

Kodi Ayuda amene anapezeka pa Pentekosite mu 33 C.E. anacokeladi “mu mtundu uliwonse mwa mitundu ya pansi pa thambo”? Kodi anthu masauzande ambili amene anali kubwela ku Yerusalemu kudzacita zikondwelelo zaciyuda anali kugona kuti?

TENGELANI CIKHULUPILILO CAWO

“Mwana Wanga Wokondedwa ndi Wokhulupilika mwa Ambuye”

N’ciani cinathandiza Timoteyo wacinyamata amene anali wamanyazi kuti akhale woyang’anila wabwino wacikristu?

Kuyankha Mafunso a m’Baibulo

Ngati akufa adzaukitsidwa, kodi adzakhala kuti?